Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anapereka nsembezo mogwirizana ndi dongosolo la tsiku ndi tsiku+ loperekera nsembe, malinga ndi chilamulo cha Mose. Nsembezo zinali za pa masabata,+ za pa masiku okhala mwezi,+ ndi za pa zikondwerero zoikidwiratu+ zochitika katatu pa chaka.+ Zikondwererozo zinali chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ chikondwerero cha masabata,+ ndi chikondwerero cha misasa.+

  • 2 Mbiri 31:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kuchokera pa katundu wake,+ mfumuyo inapereka nsembe zopsereza za m’mawa+ ndi za madzulo, komanso nsembe zopsereza za masabata,+ za masiku okhala mwezi+ ndi za panyengo zochita chikondwerero,+ monga gawo limene inayenera kupereka la nsembe zopsereza,+ mogwirizana ndi zimene zinalembedwa m’chilamulo cha Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena