Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 28:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ngakhale kuti anali kufunsira kwa Yehova,+ Yehova sanamuyankhe+ kaya kudzera m’maloto,+ Urimu+ kapena kudzera mwa aneneri.+

  • Miyambo 15:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+

  • Miyambo 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Munthu amene amathawitsa khutu lake kuti asamve chilamulo,+ ngakhale pemphero lake limakhala lonyansa.+

  • Yesaya 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+

  • Ezekieli 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Iwe mwana wa munthu, amuna awa aika mitima yawo pamafano onyansa, ndipo aika pamaso pawo chinthu chopunthwitsa chimene chimawalakwitsa.+ Kodi ndiwayankhe iwo akamandifunsa?+

  • Mika 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Oona masomphenya+ adzachita manyazi+ ndipo olosera+ adzakhumudwa ndithu. Onsewa adzaphimba ndevu zawo zapamlomo+ chifukwa Mulungu sadzawayankha.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena