Hoseya 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu anga amafunsira zinthu kwa mafano+ awo amtengo+ ndipo ndodo za m’manja mwawo zimawauza zochita. Amachita zimenezi chifukwa chakuti mtima wadama wawasocheretsa+ ndipo asiya kugonjera Mulungu wawo chifukwa cha damalo.+ Amosi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo akufunitsitsa kuti fumbi la padziko lapansi ligwere pamitu ya anthu wamba+ ndipo sakuchitira chilungamo anthu ofatsa.+ Mwana pamodzi ndi bambo ake akugona ndi mtsikana mmodzi+ ndi cholinga chofuna kuipitsa dzina langa loyera.+ Zekariya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+
12 Anthu anga amafunsira zinthu kwa mafano+ awo amtengo+ ndipo ndodo za m’manja mwawo zimawauza zochita. Amachita zimenezi chifukwa chakuti mtima wadama wawasocheretsa+ ndipo asiya kugonjera Mulungu wawo chifukwa cha damalo.+
7 Iwo akufunitsitsa kuti fumbi la padziko lapansi ligwere pamitu ya anthu wamba+ ndipo sakuchitira chilungamo anthu ofatsa.+ Mwana pamodzi ndi bambo ake akugona ndi mtsikana mmodzi+ ndi cholinga chofuna kuipitsa dzina langa loyera.+
2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+