Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 21:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako anam’bweretsera kalata+ yochokera kwa mneneri Eliya.+ Kalatayo inati: “Yehova Mulungu wa Davide kholo lanu wanena kuti, ‘Chifukwa chakuti sunayende m’njira za Yehosafati+ bambo ako, kapena m’njira za Asa+ mfumu ya Yuda,

  • Yesaya 58:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 “Fuula mwamphamvu! Usabweze mawu.+ Kweza mawu ako ngati lipenga,+ ndipo uza anthu anga za kupanduka kwawo. A nyumba ya Yakobo uwauze machimo awo.

  • Yeremiya 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Taona, lero ndakupatsa mphamvu pa mitundu ya anthu ndi maufumu,+ kuti uzule, ugwetse,+ uwononge ndi kupasula, komanso kuti umange ndi kubzala.”+

  • Ezekieli 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndachititsa chipumi chako kukhala ngati mwala wa dayamondi, cholimba kuposa mwala wa nsangalabwi.+ Usawaope,+ ndipo usachite mantha ndi nkhope zawo,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena