Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Amene akutsogolera anthuwa ndiwo amene akuwasocheretsa,+ ndipo amene akutsogoleredwawo ndiwo amene akusokonezedwa.+

  • Yesaya 56:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo sakudziwa chilichonse.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu. Satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo.+

  • Ezekieli 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 chifukwa chakuti iwo asocheretsa anthu anga ponena kuti, “Tili pa mtendere!” Koma palibe mtendere.+ Palinso munthu amene akumanga khoma lachipinda, ndipo anthu ena akulipaka laimu pachabe.’+

  • Mateyu 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Alekeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Chotero ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera m’dzenje.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena