Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Yehova akadzatsiriza ntchito yake yonse m’phiri la Ziyoni ndi mu Yerusalemu, ndidzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha zipatso za mwano wa mumtima mwake ndiponso chifukwa cha kudzikuza kwa maso ake onyada.+

  • Yesaya 37:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+

      Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+

      Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+

      Ndi Woyera wa Isiraeli!+

  • Ezekieli 38:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Udzanena kuti: “Ndipita kukaukira dziko lokhala ndi midzi yopanda mipanda.+ Ndipita kukaukira anthu amene akukhala mwabata, popanda chowasokoneza. Ndikaukira anthu onsewo amene akukhala m’midzi yopanda mipanda+ ndipo alibe zotsekera ndiponso zitseko.”

  • Yakobo 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamverani! Malipiro a anthu amene anagwira ntchito+ yokolola m’minda yanu, amene inu simunapereke,+ akufuula ndipo kufuula kwa okololawo kofuna thandizo+ kwafika m’makutu+ a Yehova wa makamu.

  • 1 Petulo 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chimodzimodzinso inu anyamata. Muzigonjera+ amuna achikulire. Koma nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa,+ chifukwa Mulungu amatsutsa odzikweza, koma odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena