Yeremiya 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira+ kudzanja langa lamanja, ndidzakuvula!+ Yohane 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Musamagwire ntchito kuti mungopeza chakudya chimene chimawonongeka,+ koma kuti mupeze chakudya chokhalitsa, chopereka moyo wosatha,+ chimene Mwana wa munthu adzakupatsani. Pakuti Atate, Mulungu yekhayo, waika chisindikizo pa iye chomuvomereza.”+ 2 Timoteyo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komabe, maziko olimba a Mulungu adakali chikhalire,+ ndipo ali ndi chidindo cha mawu akuti: “Yehova* amadziwa anthu ake,”+ ndiponso akuti: “Aliyense wotchula dzina la Yehova+ aleke kuchita zosalungama.”+
24 “‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira+ kudzanja langa lamanja, ndidzakuvula!+
27 Musamagwire ntchito kuti mungopeza chakudya chimene chimawonongeka,+ koma kuti mupeze chakudya chokhalitsa, chopereka moyo wosatha,+ chimene Mwana wa munthu adzakupatsani. Pakuti Atate, Mulungu yekhayo, waika chisindikizo pa iye chomuvomereza.”+
19 Komabe, maziko olimba a Mulungu adakali chikhalire,+ ndipo ali ndi chidindo cha mawu akuti: “Yehova* amadziwa anthu ake,”+ ndiponso akuti: “Aliyense wotchula dzina la Yehova+ aleke kuchita zosalungama.”+