Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa za pamalo anga odyetsera ziweto!”+ watero Yehova.

  • Ezekieli 22:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Aneneri ako akukonza chiwembu mwa iwe.+ Iwo akukhadzula anthu+ ngati mkango wobangula umene wagwira nyama.+ Akulanda anthu chuma ndi zinthu zawo zamtengo wapatali.+ Achulukitsa akazi amasiye mmenemo.+

  • Ezekieli 34:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, losera zoipa zimene zidzachitikire abusa a Isiraeli. Losera, ndipo uuze abusawo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka abusa a Isiraeli,+ amene akungodzidyetsa okha!+ Kodi abusa ntchito yawo si kudyetsa nkhosa?+

  • Mika 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Inu mumadana ndi zinthu zabwino+ ndi kukonda zinthu zoipa.+ Mumasenda khungu la anthu ndi kuchotsa mnofu pamafupa awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena