Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye ananyozedwa ndipo anthu anali kumupewa.+ Anali munthu amene anadziwa kupweteka ndiponso amene anadziwa matenda.+ Ife tinali kuyang’ana kumbali kuti tisaone nkhope yake.+ Ananyozedwa ndipo tinamuona ngati wopanda pake.+

  • Mateyu 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Atatero, alembi ena anang’ung’udza chamumtima kuti: “Munthu ameneyu akunyoza Mulungu.”+

  • Maliko 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “N’chifukwa chiyani munthu ameneyu akulankhula chonchi? Akunyoza Mulungu ameneyu. Ndaninso wina amene angakhululukire machimo, si Mulungu yekha kodi?”+

  • Luka 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pamenepo alembi ndi Afarisi anayamba kudzifunsa, kuti: “Ndani ameneyu kuti azinyoza Mulungu chonchi?+ Winanso ndani amene angakhululukire machimo? Si Mulungu yekha kodi?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena