Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Atesalonika 5
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la 1 Atesalonika

      • Kubwera kwa tsiku la Yehova (1-5)

        • “Bata ndi mtendere!” (3)

      • Khalanibe maso komanso oganiza bwino (6-11)

      • Kuwalimbikitsa (12-24)

      • Moni womaliza (25-28)

1 Atesalonika 5:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1986, tsa. 27

1 Atesalonika 5:2

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zef 1:14
  • +Mt 24:36; 2Pe 3:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, ptsa. 8-9

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, ptsa. 8-9

    9/2019, tsa. 9

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 222

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2012, tsa. 3

    7/15/2010, tsa. 5

    5/1/2009, tsa. 14

    5/15/2008, ptsa. 15-16

    11/1/1988, tsa. 6

    10/1/1986, ptsa. 27-29, 30-31

1 Atesalonika 5:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 37:10; Yer 8:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2023, tsa. 21

    6/2023, ptsa. 9, 13

    2/2023, tsa. 16

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, ptsa. 8-9

    9/2019, ptsa. 9-10

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 222-223

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2013, ptsa. 12-13

    1/1/2013, tsa. 7

    9/15/2012, tsa. 3

    7/15/2010, tsa. 5

    5/15/2008, ptsa. 15-16

    2/1/2004, ptsa. 20-21

    6/1/1997, ptsa. 9-10

    4/15/1995, tsa. 25

    8/1/1994, tsa. 6

    9/15/1991, tsa. 16

    9/1/1991, ptsa. 5-6, 7-8

    4/15/1991, tsa. 7

    11/1/1988, tsa. 6

    9/1/1987, ptsa. 18-20, 23

    5/15/1987, ptsa. 17-19

    10/1/1986, ptsa. 29-31

    Galamukani!,

    4/2008, tsa. 7

    12/8/1989, ptsa. 28-31

    5/8/1988, tsa. 14

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 250-251

    Lambirani Mulungu, tsa. 182

    Mulungu Amatisamaliradi?, tsa. 21

    Chifuno cha Moyo, tsa. 28

    Mtendere Weniweni, ptsa. 5-7, 84-85

1 Atesalonika 5:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, ptsa. 9-10

1 Atesalonika 5:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 12:36; Aro 13:12; Aef 5:8
  • +Yoh 8:12; Akl 1:13; 1Pe 2:9

1 Atesalonika 5:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 13:11
  • +Mt 24:42
  • +1Pe 5:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2019, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2012, ptsa. 10-11

    1/1/2003, tsa. 11

    10/1/1989, tsa. 30

1 Atesalonika 5:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 13:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, tsa. 10

1 Atesalonika 5:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 6:14-17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, ptsa. 10-12

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2022, ptsa. 25-26

    Mulungu Azikukondani, tsa. 232

    ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 202-203

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2013, tsa. 11

    12/15/2008, ptsa. 6-7

    10/1/2006, tsa. 29

    1/1/2003, ptsa. 20-22

    6/1/2000, ptsa. 9-10

    4/15/1993, ptsa. 11-13

    1/15/1991, tsa. 22

    7/15/1989, tsa. 19

    Galamukani!,

    5/8/2004, tsa. 20

1 Atesalonika 5:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2At 2:13

1 Atesalonika 5:10

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “tigona mu imfa.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 5:8
  • +1At 4:16, 17

1 Atesalonika 5:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 1:11, 12; 15:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, ptsa. 11-12

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    8/2022, ptsa. 20-25

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 48

    Utumiki wa Ufumu,

    9/2006, tsa. 3

1 Atesalonika 5:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2011, ptsa. 24-28

    6/1/1999, tsa. 18

    8/15/1991, tsa. 19

    10/1/1988, ptsa. 15-16

1 Atesalonika 5:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 2:29, 30; 1Ti 5:17; Ahe 13:7
  • +Mko 9:50; 2Ak 13:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1999, ptsa. 18-19

    8/15/1991, tsa. 19

    10/1/1988, ptsa. 15-16

1 Atesalonika 5:14

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “muzilangiza.”

  • *

    Kapena kuti, “amene afooka.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Le 19:17; 2Ti 4:2
  • +1Ak 13:4; Aga 5:22; Aef 4:1, 2; Akl 3:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 1 2023 ptsa. 14-15

    Yandikirani, ptsa. 102-103, 166-167

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2017, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2015, tsa. 9

    8/15/2013, tsa. 22

    6/15/2010, ptsa. 12-13

    5/1/2004, tsa. 21

    11/1/2001, ptsa. 17-18

    10/1/1995, ptsa. 15-16

    3/15/1990, ptsa. 26-28

    Galamukani!,

    10/2013, tsa. 14

    7/2009, ptsa. 7-9

    Chinsinsi cha Banja, ptsa. 36-37

1 Atesalonika 5:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 5:39
  • +Aro 12:17, 19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/1990, tsa. 28

1 Atesalonika 5:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 6:4, 10; Afi 4:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1991, ptsa. 8-10

1 Atesalonika 5:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 18:1; Aro 12:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/2010, tsa. 9

    9/15/2003, ptsa. 15-20

    5/15/1990, tsa. 16

1 Atesalonika 5:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 5:20; Akl 3:17

1 Atesalonika 5:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 4:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, ptsa. 12-13

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/2000, tsa. 10

    12/1/1989, tsa. 21

1 Atesalonika 5:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 14:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, ptsa. 12-13

1 Atesalonika 5:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 4:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    6/2023, tsa. 13

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1996, tsa. 17

    Galamukani!,

    2/8/1996, tsa. 6

1 Atesalonika 5:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 2:3

1 Atesalonika 5:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 1:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2008, tsa. 29

    5/1/1993, tsa. 11

1 Atesalonika 5:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 15:30

1 Atesalonika 5:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 4:16

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

1 Ates. 5:2Zef 1:14
1 Ates. 5:2Mt 24:36; 2Pe 3:10
1 Ates. 5:3Sl 37:10; Yer 8:11
1 Ates. 5:5Yoh 12:36; Aro 13:12; Aef 5:8
1 Ates. 5:5Yoh 8:12; Akl 1:13; 1Pe 2:9
1 Ates. 5:6Aro 13:11
1 Ates. 5:6Mt 24:42
1 Ates. 5:61Pe 5:8
1 Ates. 5:7Aro 13:13
1 Ates. 5:8Aef 6:14-17
1 Ates. 5:92At 2:13
1 Ates. 5:10Aro 5:8
1 Ates. 5:101At 4:16, 17
1 Ates. 5:11Aro 1:11, 12; 15:2
1 Ates. 5:13Afi 2:29, 30; 1Ti 5:17; Ahe 13:7
1 Ates. 5:13Mko 9:50; 2Ak 13:11
1 Ates. 5:14Le 19:17; 2Ti 4:2
1 Ates. 5:141Ak 13:4; Aga 5:22; Aef 4:1, 2; Akl 3:13
1 Ates. 5:15Mt 5:39
1 Ates. 5:15Aro 12:17, 19
1 Ates. 5:162Ak 6:4, 10; Afi 4:4
1 Ates. 5:17Lu 18:1; Aro 12:12
1 Ates. 5:18Aef 5:20; Akl 3:17
1 Ates. 5:19Aef 4:30
1 Ates. 5:201Ak 14:1
1 Ates. 5:211Yo 4:1
1 Ates. 5:22Yob 2:3
1 Ates. 5:231Ak 1:8
1 Ates. 5:25Aro 15:30
1 Ates. 5:27Akl 4:16
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Atesalonika 5:1-28

Kalata Yoyamba Yopita kwa Atesalonika

5 Koma tsopano za nthawi ndi nyengo abale, simukufunika kuti tikulembereni chilichonse. 2 Chifukwa inuyo mukudziwa bwino kuti tsiku la Yehova*+ lidzabwera ndendende ngati wakuba usiku.+ 3 Akadzangonena kuti, “Bata ndi mtendere!” nthawi yomweyo adzawonongedwa. Tsoka limeneli lidzawagwera modzidzimutsa+ ngati ululu umene mkazi woyembekezera amamva akatsala pangʼono kubereka ndipo sadzapulumuka. 4 Koma inu abale simuli mumdima kuti tsiku limenelo lidzakudzidzimutseni ngati mmene akuba amadzidzimukira kunja kukawachera. 5 Chifukwa nonsenu ndi ana a kuwala ndiponso ana a masana.+ Si ife a usiku kapena a mdima.+

6 Choncho tisapitirize kugona ngati mmene ena onse akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+ 7 Chifukwa amene akugona amagona usiku ndipo amene amaledzera, amaledzera usiku.+ 8 Koma ife amene tili a masana, tikhalebe oganiza bwino ndipo tivale chodzitetezera pachifuwa cha chikhulupiriro ndi chikondi. Tivalenso chiyembekezo cha chipulumutso ngati chipewa,+ 9 chifukwa Mulungu sanatisankhe kuti adzatilange, koma anatisankha kuti tidzapulumuke+ chifukwa cha zimene Ambuye wathu Yesu Khristu anachita. 10 Iye anatifera,+ kuti kaya tikhala maso kapena tigona,* tikhale ndi moyo limodzi ndi iye.+ 11 Choncho pitirizani kutonthozana ndi kulimbikitsana+ ngati mmene mukuchitira.

12 Tsopano tikukupemphani abale, kuti muzilemekeza anthu amene akugwira ntchito mwakhama pakati panu, amenenso amakutsogolerani mwa Ambuye komanso kukulangizani. 13 Muziwasonyeza chikondi komanso ulemu waukulu chifukwa cha ntchito yawo.+ Muzikhala mwamtendere pakati panu.+ 14 Komanso tikukulimbikitsani abale, kuti muzichenjeza* anthu ochita zosalongosoka,+ muzilankhula molimbikitsa kwa anthu amene ali ndi nkhawa,* muzithandiza ofooka, muzikhala oleza mtima kwa onse.+ 15 Onetsetsani kuti pasapezeke wobwezera choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse muziyesetsa kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+

16 Muzikhala osangalala nthawi zonse.+ 17 Muzipemphera nthawi zonse.+ 18 Muzithokoza pa chilichonse.+ Mulungu akufuna kuti muzichita zimenezi chifukwa ndinu otsatira a Khristu Yesu. 19 Musazimitse moto wa mzimu.+ 20 Musamanyoze mawu aulosi.+ 21 Muzifufuza zinthu zonse nʼkutsimikizira zimene zili zabwino+ ndipo gwirani mwamphamvu zabwinozo. 22 Muzipewa zoipa zamtundu uliwonse.+

23 Mulungu wamtendereyo akupatuleni kuti muchite utumiki wake. Ndipo pa mbali zonse abale, mzimu wanu, moyo wanu komanso thupi lanu, zikhale zopanda chilema kapena cholakwa chilichonse, pa nthawi ya kukhalapo kwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+ 24 Amene akukuitanani ndi wokhulupirika ndipo adzachitadi zimenezi.

25 Abale, pitirizani kutipempherera.+

26 Mupereke moni kwa abale onse ndipo mukisane ndi mtima woyera.

27 Ndikukupemphani mwa Ambuye kuti kalatayi iwerengedwe kwa abale onse.+

28 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu Khristu kukhale nanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena