Ndandanda ya Mlungu wa March 12
MLUNGU WOYAMBIRA MARCH 12
Nyimbo Na. 99 ndi Pemphero
□ Phunziro la Baibulo la Mpingo:
bt mutu 3 ndime 4-11 (Mph. 25)
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Yeremiya 5-7 (Mph. 10)
Na. 1: Yeremiya 5:15-25 (Osapitirira mph. 4)
Na. 2: N’chifukwa Chiyani Kale Mulungu Ankalola Munthu Kukwatirana ndi Mlongo Wake?—rs tsa. 387 ndime 2-3 (Mph. 5)
Na. 3: Kodi Yehova Amateteza Bwanji Anthu Ake Mwauzimu? (Mph. 5)
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Kulitsani Luso la Kuphunzitsa—Gawo 2. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, tsamba 57 ndime 3 mpaka pa kamutu ka patsamba 59.
Mph. 10: Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2011. Nkhani yokambirana yochokera pa Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2011 limene lili patsamba 3 mpaka 6. Fotokozani mbali zimene zinapita patsogolo kwambiri pa ntchito yathu yolalikira padziko lonse m’chaka chautumiki chapitachi.
Mph. 10: “Muzichita Zimenezi.” Mafunso ndi mayankho. Dziwitsani mpingo za malo ndi nthawi yochitira Chikumbutso.
Nyimbo Na. 109 ndi Pemphero