Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Anthu asanu mwa inu adzathamangitsa adani 100, ndipo anthu 100 adzathamangitsa adani 10,000, moti mudzagonjetsa adani anu ndi lupanga.+

  • Oweruza 3:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pambuyo pa Ehudi panadzakhala Samagara+ mwana wamwamuna wa Anati. Ameneyu anapha amuna achifilisiti+ 600 ndi chisonga chotosera ng’ombe pozitsogolera. Ameneyunso anapulumutsa Isiraeli.+

  • 1 Samueli 14:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho Yonatani anauza mtumiki wake womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa amuna osadulidwawa.+ Pakuti mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa anthu ake pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+

  • 2 Samueli 23:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mayina a amuna amphamvu+ a Davide ndi awa: Yosebu-basebete+ Mtahakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu. Iye anatenga mkondo wake n’kupha anthu 800 ulendo umodzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena