Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,

      Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+

      Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+

      Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+

  • 1 Samueli 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Nthawi yomweyo, Davide anauza amuna amene anali kuyenda naye kuti: “Aliyense amange lupanga lake m’chiuno!”+ Pamenepo aliyense anamangadi lupanga lake m’chiuno, ndipo Davide nayenso anamanga lupanga lake m’chiuno. Zitatero, amuna pafupifupi 400 anapitira limodzi ndi Davide, koma amuna 200 anatsala kuti ayang’anire katundu.+

  • Salimo 45:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mangirira lupanga lako+ m’chiuno mwako wamphamvu iwe,+

      Limodzi ndi ulemu ndiponso ulemerero wako.+

  • Miyambo 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Usadzitame ndi zamawa+ chifukwa sukudziwa zimene zidzachitike mawa.+

  • Mlaliki 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mapeto a chinthu amakhala bwino kuposa chiyambi chake,+ ndipo munthu woleza mtima ndi wabwino kuposa munthu wodzikuza.+

  • Mlaliki 8:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pakuti palibe akudziwa zimene zidzachitike,+ popeza ndani angamuuze mmene zidzachitikire?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena