Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:

      “Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+

      Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+

      Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,

      Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+

  • Nehemiya 12:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Pa tsiku limenelo anapereka nsembe zochuluka+ ndipo anasangalala+ pakuti Mulungu woona anawachititsa kusangalala kwambiri.+ Akazi+ ndi ana+ nawonso anasangalala, mwakuti phokoso la chisangalalo cha Yerusalemu linamveka kutali.+

  • Salimo 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tidzafuula mokondwera chifukwa cha chipulumutso chanu,+

      Tidzakweza mbendera zathu m’dzina la Mulungu wathu.+

      Yehova akwaniritse zopempha zanu zonse.+

  • Salimo 30:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndidzakutamandani inu Yehova, pakuti mwandipulumutsa,+

      Ndipo simunalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena