Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ndipo patebulopo uziikapo mkate wachionetsero pamaso panga nthawi zonse.+

  • Levitiko 24:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo usanjikize mikateyo m’magulu awiri. Gulu lililonse likhale ndi mikate 6.+ Uike mikateyo patebulo lagolide woyenga bwino pamaso pa Yehova.+

  • 1 Mbiri 23:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Anali kutumidwanso pa ntchito zokhudza mkate wosanjikiza,+ ufa wosalala+ wa nsembe yambewu, mikate yopyapyala+ yopanda chofufumitsa,+ makeke ophika m’chiwaya,+ ufa wokanya wosakaniza ndi mafuta,+ ndiponso miyezo yosiyanasiyana.+

  • Mateyu 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena