Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+

  • Deuteronomo 30:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Musankhe moyo mwa kukonda Yehova Mulungu wanu,+ kumvera mawu ake ndi kum’mamatira,+ chifukwa iye ndiye wokupatsani moyo ndi masiku ambiri+ kuti mukhale panthaka imene Yehova analumbira kwa makolo anu, Abulahamu, Isaki ndi Yakobo kuti adzawapatsa.”+

  • Salimo 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+

      Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+

  • Salimo 91:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndidzamukhutiritsa ndi masiku ambiri,+

      Ndipo ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+

  • Mateyu 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma chipata cholowera ku moyo n’chopapatiza komanso msewu wake ndi wopanikiza, ndipo amene akuupeza ndi owerengeka.+

  • 1 Petulo 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti “amene akufuna kusangalala ndi moyo ndi kuona masiku abwino,+ aletse lilime+ lake kuti lisalankhule zoipa ndi milomo yake kuti isalankhule chinyengo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena