Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 33:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Manase anayamba kupemphera kwa Mulungu ndipo iye anamva kupembedzera kwake+ ndi pempho lake lopempha chifundo. Kenako anam’bwezera ku Yerusalemu ku ufumu wake,+ ndipo Manase anadziwa kuti Yehova ndiye Mulungu woona.+

  • Salimo 22:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pakuti iye sananyoze,+

      Kapena kunyansidwa ndi nsautso ya munthu wosautsidwa.+

      Ndipo sanam’bisire nkhope yake.+

      Pamene anamulirira kuti amuthandize, iye anamva.+

  • Salimo 119:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  58 Ndayesetsa ndi mtima wanga wonse kuti mundiyanje.*+

      Ndikomereni mtima monga mwa mawu anu.+

  • Miyambo 28:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+ koma woulula n’kuwasiya adzachitiridwa chifundo.+

  • Luka 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma bambowo anauza akapolo ake kuti, ‘Fulumirani, tengani mkanjo wabwino kwambiri uja mumuveke!+ Mumuvekenso mphete+ kudzanja lake ndi nsapato kumapazi kwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena