Salimo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+ Salimo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’kamwa mwa ana aang’ono ndi ana oyamwa mwakhazikitsamo zamphamvu,+Chifukwa cha amene akukuchitirani zoipa.+Mwatero kuti mugonjetse mdani wanu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa.+ Salimo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zochita zake zimayenda bwino nthawi zonse.+Zigamulo zanu zili pamwamba kwambiri pamene iye sangathe kuziona.+Onse omuchitira zoipa amawanyodola.+
2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+ Salimo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’kamwa mwa ana aang’ono ndi ana oyamwa mwakhazikitsamo zamphamvu,+Chifukwa cha amene akukuchitirani zoipa.+Mwatero kuti mugonjetse mdani wanu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa.+ Salimo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zochita zake zimayenda bwino nthawi zonse.+Zigamulo zanu zili pamwamba kwambiri pamene iye sangathe kuziona.+Onse omuchitira zoipa amawanyodola.+
2 M’kamwa mwa ana aang’ono ndi ana oyamwa mwakhazikitsamo zamphamvu,+Chifukwa cha amene akukuchitirani zoipa.+Mwatero kuti mugonjetse mdani wanu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa.+
5 Zochita zake zimayenda bwino nthawi zonse.+Zigamulo zanu zili pamwamba kwambiri pamene iye sangathe kuziona.+Onse omuchitira zoipa amawanyodola.+