Yobu 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ana ake amalemekezedwa, koma iye sadziwa zimenezo.+Iwo amakhala opanda pake, koma iye sawaganizira. Mlaliki 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndani angadziwe zabwino zimene munthu angachite pa moyo wake,+ masiku onse a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Pakuti ndani angamuuze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?+ Mlaliki 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo chitsiru chimalankhula mawu ambiri.+ Munthu sadziwa chimene chidzachitike, ndipo ndani angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+
21 Ana ake amalemekezedwa, koma iye sadziwa zimenezo.+Iwo amakhala opanda pake, koma iye sawaganizira.
12 Ndani angadziwe zabwino zimene munthu angachite pa moyo wake,+ masiku onse a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Pakuti ndani angamuuze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?+
14 Ndipo chitsiru chimalankhula mawu ambiri.+ Munthu sadziwa chimene chidzachitike, ndipo ndani angamuuze zimene zidzachitike iye atafa?+