Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 24:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mwambi wa anthu akale umati, ‘Choipa chimachokera kwa munthu woipa,’+ koma dzanja langali silidzakukhudzani.

  • 1 Samueli 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Davide anapitiriza kunena kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ Yehova iye mwini adzamukantha,+ kapena tsiku lidzafika+ ndipo adzamwalira mmene amachitira wina aliyense, kapenanso adzapita kunkhondo+ ndipo adzaphedwa kumeneko.+

  • 1 Mbiri 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 A fuko la Isakara,+ amene anali ndi nzeru zotha kudziwa nthawi,+ ndi zimene Aisiraeli ayenera kuchita,+ analipo atsogoleri 200, ndipo iwo anali kulamulira abale awo onse.

  • Salimo 37:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Khala chete pamaso pa Yehova,+

      Ndipo umuyembekezere ndi mtima wako wonse.+

      Usapse mtima ndi aliyense amene zinthu zikumuyendera bwino,+

      Munthu amene akukwaniritsa zolinga zake zoipa.+

  • Miyambo 17:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Nzeru zimakhala pamaso pa munthu womvetsa zinthu,+ koma maso a munthu wopusa ali kumalekezero a dziko lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena