Salimo 112:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wachisomo+ komanso wokongoza ena zinthu ndi wabwino.+ י [Yohdh]Amachita zinthu mwachilungamo.+ Miyambo 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+ Yesaya 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Taonani! Mfumu+ idzalamulira mwachilungamo,+ ndipo akalonga+ adzalamuliranso mwachilungamo. Mika 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+
5 Munthu wachisomo+ komanso wokongoza ena zinthu ndi wabwino.+ י [Yohdh]Amachita zinthu mwachilungamo.+
4 Pochita zinthu zachilungamo, mfumu imachititsa dziko kulimba,+ koma munthu wokonda ziphuphu amaligwetsa.+
8 Iwe munthu wochokera kufumbi, iye anakuuza zimene zili zabwino.+ Kodi Yehova akufuna chiyani kwa iwe? Iye akufuna kuti uzichita chilungamo,+ ukhale wokoma mtima+ ndiponso uziyenda modzichepetsa+ ndi Mulungu wako.+