Salimo 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndamva zinthu zoipa zimene anthu ambiri akunena,+Ndamva zochititsa mantha kuchokera kumbali zonse.+Akasonkhana pamodzi kundichitira upo,+Amakonza chiwembu kuti achotse moyo wanga.+ Yeremiya 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Musatuluke kupita kunja ndipo musayende m’njira pakuti kumeneko kuli lupanga la mdani. Zochititsa mantha zili paliponse.+ Yeremiya 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘N’chifukwa chiyani akuoneka kuti agwidwa ndi mantha? Akubwerera, ndipo amuna awo amphamvu aphwanyika ndi kukhala zidutswazidutswa. Iwo athawadi ndipo sanacheuke.+ Zochititsa mantha zili paliponse,’+ watero Yehova. Yeremiya 49:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mahema awo,+ nkhosa zawo,+ nsalu za mahema awo ndi zinthu zawo zonse zidzatengedwa.+ Ngamila zawo+ zidzalandidwa. Anthu adzawalirira kuti, ‘Zochititsa mantha zili paliponse!’”+ Maliro 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munaitana+ anthu kuchokera kumalo onse ozungulira, kumene akukhala monga alendo.Pa tsiku la mkwiyo wa Yehova panalibe wothawa kapena wopulumuka.+Ana onse athanzi amene ndinabereka ndi kuwalera, mdani wanga anawapha.+
13 Ndamva zinthu zoipa zimene anthu ambiri akunena,+Ndamva zochititsa mantha kuchokera kumbali zonse.+Akasonkhana pamodzi kundichitira upo,+Amakonza chiwembu kuti achotse moyo wanga.+
25 Musatuluke kupita kunja ndipo musayende m’njira pakuti kumeneko kuli lupanga la mdani. Zochititsa mantha zili paliponse.+
5 “‘N’chifukwa chiyani akuoneka kuti agwidwa ndi mantha? Akubwerera, ndipo amuna awo amphamvu aphwanyika ndi kukhala zidutswazidutswa. Iwo athawadi ndipo sanacheuke.+ Zochititsa mantha zili paliponse,’+ watero Yehova.
29 Mahema awo,+ nkhosa zawo,+ nsalu za mahema awo ndi zinthu zawo zonse zidzatengedwa.+ Ngamila zawo+ zidzalandidwa. Anthu adzawalirira kuti, ‘Zochititsa mantha zili paliponse!’”+
22 Munaitana+ anthu kuchokera kumalo onse ozungulira, kumene akukhala monga alendo.Pa tsiku la mkwiyo wa Yehova panalibe wothawa kapena wopulumuka.+Ana onse athanzi amene ndinabereka ndi kuwalera, mdani wanga anawapha.+