27 M’tsiku limenelo, Yehova+ adzagwiritsa ntchito lupanga lake lakuthwa,+ lalikulu ndi lochititsa mantha kupha Leviyatani,+ njoka yokwawa mwamyaa!+ Ndithu adzapha Leviyatani, njoka yoyenda mothamanga ndi mokhotakhota, ndipo adzapha chinjoka chachikulu chokhala m’nyanja.+