Danieli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Idzalankhula mawu otsutsana ndi Wam’mwambamwamba+ ndipo idzazunza mosalekeza oyera a Wamkulukulu.+ Idzafuna kusintha nthawi+ ndiponso lamulo+ ndipo oyerawo adzaperekedwa m’manja mwake kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi.+ Chivumbulutso 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma bwalo lakunja+ kwa nyumba yopatulika ya pakachisi ulisiye, usaliyeze m’pang’ono pomwe chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+ Chivumbulutso 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma mkaziyo anathawira kuchipululu,+ kumene Mulungu anamukonzera malo, kuti akadyetsedwe+ masiku 1,260.+ Chivumbulutso 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri+ a chiwombankhanga chachikulu kuti aulukire kuchipululu,+ kumalo ake aja. Kumeneko n’kumene akudyetsedwa+ kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi njoka ija.+ Chivumbulutso 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chilombocho chinapatsidwa pakamwa polankhula zinthu zodzitukumula+ ndi zonyoza.+ Chinapatsidwanso mphamvu yochita ulamuliro kwa miyezi 42.+
25 Idzalankhula mawu otsutsana ndi Wam’mwambamwamba+ ndipo idzazunza mosalekeza oyera a Wamkulukulu.+ Idzafuna kusintha nthawi+ ndiponso lamulo+ ndipo oyerawo adzaperekedwa m’manja mwake kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi.+
2 Koma bwalo lakunja+ kwa nyumba yopatulika ya pakachisi ulisiye, usaliyeze m’pang’ono pomwe chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+
6 Koma mkaziyo anathawira kuchipululu,+ kumene Mulungu anamukonzera malo, kuti akadyetsedwe+ masiku 1,260.+
14 Koma mkaziyo anapatsidwa mapiko awiri+ a chiwombankhanga chachikulu kuti aulukire kuchipululu,+ kumalo ake aja. Kumeneko n’kumene akudyetsedwa+ kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi,+ kutali ndi njoka ija.+
5 Chilombocho chinapatsidwa pakamwa polankhula zinthu zodzitukumula+ ndi zonyoza.+ Chinapatsidwanso mphamvu yochita ulamuliro kwa miyezi 42.+