Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 22:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “Usatemberere Mulungu+ kapena kutemberera mtsogoleri amene ali pakati pa anthu ako.+

  • Yohane 17:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Komanso, ndawapatsa ulemerero umene munandipatsa, kuti iwo akhale amodzi mmene ifenso tilili amodzi.+

  • 1 Timoteyo 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 munthu ameneyo ndi wodzitukumula ndiponso wonyada,+ ndipo samvetsa kanthu kalikonse.+ M’malomwake, amakonda kukangana ndi anthu ndiponso kutsutsana pa mawu.+ Zimenezi zimayambitsa kaduka,+ mikangano, kunenerana mawu achipongwe,+ ndiponso kuganizirana zoipa.

  • 1 Petulo 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu,+ ndinu odala+ chifukwa zikusonyeza kuti mzimu waulemerero, umene ndi mzimu wa Mulungu, wakhazikika pa inu.+

  • 3 Yohane 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 N’chifukwa chake ndikadzabwera, ndidzaulula ntchito zake zimene akupitirizabe kuchita.+ Iye amatinenera zamwano,+ komanso chifukwa chosakhutira ndi zinthu zimenezi, iye salandira abalewo+ mwaulemu, ndipo amene amafuna kulandira+ abalewo, amawatsekereza+ ndi kuwachotsa+ mumpingo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena