Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 21
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 21:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 65:17; 2Pe 3:13
  • +Yes 66:22
  • +2Pe 3:10
  • +Chv 20:11
  • +Yes 57:20; Chv 17:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    11/2023, tsa. 4

    Kufotokoza Mavesi a m’Baibulo, article 33

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 301

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2001, tsa. 31

    4/15/2000, tsa. 12

    7/15/1991, ptsa. 5-6

    9/15/1990, tsa. 6

    Galamukani!,

    1/8/1997, tsa. 31

    Kukambitsirana, ptsa. 133-134

Chivumbulutso 21:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 52:1
  • +Ahe 12:22; Chv 3:12
  • +Chv 19:7
  • +Mt 9:15; Yoh 3:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2010, ptsa. 4-5

    7/1/1995, ptsa. 13-14

    1/1/1993, tsa. 7

    7/15/1991, ptsa. 5-6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 301-303

    Kukambitsirana, tsa. 134

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 92-93, 95-97

Chivumbulutso 21:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 37:27
  • +Sl 15:1
  • +Yes 66:23
  • +Eze 43:7; 48:35

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 26

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2013, tsa. 23

    7/15/1991, ptsa. 5-6

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 303

    Kukambitsirana, tsa. 134

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 177-178

    “Tawonani!,” ptsa. 29-30

Chivumbulutso 21:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 65:19; Chv 7:17
  • +Yes 25:8; 1Ak 15:26
  • +Yes 35:10; 65:19
  • +2Pe 3:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 2

    Galamukani!,

    No. 1 2021 tsa. 13

    7/8/1994, ptsa. 21-22, 27-28

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/2013, tsa. 11

    9/15/2012, tsa. 10

    8/1/2012, tsa. 22

    1/15/2012, tsa. 30

    12/1/2009, ptsa. 5-6

    8/15/2006, tsa. 31

    4/15/2000, ptsa. 12-13

    7/15/1990, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 303

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 177-178

    “Tawonani!,” ptsa. 29-30

Chivumbulutso 21:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Mb 18:18; Yes 6:1; Chv 4:2
  • +Yes 42:9; Mlr 5:21; Eze 36:26; 2Pe 3:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    11/2023, ptsa. 3-4

    Yandikirani, ptsa. 81-86

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 303-304

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2000, tsa. 14

    7/15/1991, ptsa. 5-6

    3/1/1987, ptsa. 28-32

Chivumbulutso 21:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:8; 22:13
  • +Sl 36:9; Yes 55:1; Chv 7:17; 22:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    11/2023, ptsa. 3, 4-7

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2016, ptsa. 21-22

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 303-304

Chivumbulutso 21:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 15:28; Chv 3:12
  • +2Sa 7:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 304

Chivumbulutso 21:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 11:20; Ahe 3:19; 1Yo 5:10
  • +Aro 1:24; 1Ak 6:9
  • +1Yo 3:15
  • +Aef 5:5
  • +Aga 5:20
  • +Yoh 8:44; Mac 5:3; 1Ti 1:10
  • +Mt 5:22; 18:9; Yak 3:6
  • +Yes 30:33; Mt 10:28; Chv 19:20
  • +Miy 10:7; Ahe 10:26; Chv 2:11; 20:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2148

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 304-305

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1987, ptsa. 24-25

Chivumbulutso 21:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Le 26:21; Chv 15:1
  • +Sl 45:9; Chv 19:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2007, tsa. 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 305-306

Chivumbulutso 21:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 2:2; Eze 40:2; Mik 4:1
  • +Yes 52:1
  • +Ahe 12:22; Chv 3:12; 21:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 305-306

Chivumbulutso 21:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 60:1
  • +Eks 24:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 302, 305-306

Chivumbulutso 21:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 60:18
  • +Eks 28:21; 39:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 302, 306

Chivumbulutso 21:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 22:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 302, 306

Chivumbulutso 21:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 11:10
  • +Mt 10:2; Lu 6:13; Mac 1:13; Aef 2:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 302, 306

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1997, ptsa. 13-14

Chivumbulutso 21:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 40:3; Chv 11:1
  • +Eze 40:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 306

Chivumbulutso 21:16

Mawu a M'munsi

  • *

    Makilomita pafupifupi 2,200. Onani mawu a m’munsi pa Chv 14:20.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 306-307

Chivumbulutso 21:17

Mawu a M'munsi

  • *

    Mamita pafupifupi 64.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 306-307

Chivumbulutso 21:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:3; 21:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 307-308

Chivumbulutso 21:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 54:11
  • +Yes 54:12
  • +Eks 28:18; Eze 28:13
  • +Eks 39:11; Yob 28:6
  • +Eks 28:17; Chv 4:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 307-308

Chivumbulutso 21:20

Mawu a M'munsi

  • *

    Yonseyi ndi miyala yamtengo wapatali yamitundu yosiyanasiyana, ndipo ina ndi yokhala ndi mitundu ingapo yosiyana m’mwala umodzi.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 28:20; Nym 5:14; Eze 1:16; Da 10:6
  • +Eks 28:17; 39:10; Yob 28:19; Eze 28:13
  • +Eks 28:19; 39:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 307-308

Chivumbulutso 21:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Est 1:6; Yob 28:18; Mt 13:46

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 307-308

Chivumbulutso 21:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 7:49
  • +Sl 11:4
  • +Eks 6:3; Chv 15:3
  • +Yoh 4:23
  • +Aef 2:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 17-18

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 308-309

Chivumbulutso 21:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 60:19; Chv 22:5
  • +Yoh 1:9; Mac 26:13; Ahe 1:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 308-309

Chivumbulutso 21:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 60:3
  • +Sl 138:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 310

Chivumbulutso 21:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 60:11
  • +Yes 60:20

Chivumbulutso 21:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 60:5

Chivumbulutso 21:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 6:9; Aga 5:21
  • +Sl 5:6; Akl 3:9; Chv 21:8
  • +Yes 52:1
  • +Da 12:1; Afi 4:3; Chv 13:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 306, 310

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 21:1Yes 65:17; 2Pe 3:13
Chiv. 21:1Yes 66:22
Chiv. 21:12Pe 3:10
Chiv. 21:1Chv 20:11
Chiv. 21:1Yes 57:20; Chv 17:15
Chiv. 21:2Yes 52:1
Chiv. 21:2Ahe 12:22; Chv 3:12
Chiv. 21:2Chv 19:7
Chiv. 21:2Mt 9:15; Yoh 3:29
Chiv. 21:3Eze 37:27
Chiv. 21:3Sl 15:1
Chiv. 21:3Yes 66:23
Chiv. 21:3Eze 43:7; 48:35
Chiv. 21:4Yes 65:19; Chv 7:17
Chiv. 21:4Yes 25:8; 1Ak 15:26
Chiv. 21:4Yes 35:10; 65:19
Chiv. 21:42Pe 3:7
Chiv. 21:52Mb 18:18; Yes 6:1; Chv 4:2
Chiv. 21:5Yes 42:9; Mlr 5:21; Eze 36:26; 2Pe 3:13
Chiv. 21:6Chv 1:8; 22:13
Chiv. 21:6Sl 36:9; Yes 55:1; Chv 7:17; 22:1
Chiv. 21:71Ak 15:28; Chv 3:12
Chiv. 21:72Sa 7:14
Chiv. 21:8Aro 11:20; Ahe 3:19; 1Yo 5:10
Chiv. 21:8Aro 1:24; 1Ak 6:9
Chiv. 21:81Yo 3:15
Chiv. 21:8Aef 5:5
Chiv. 21:8Aga 5:20
Chiv. 21:8Yoh 8:44; Mac 5:3; 1Ti 1:10
Chiv. 21:8Mt 5:22; 18:9; Yak 3:6
Chiv. 21:8Yes 30:33; Mt 10:28; Chv 19:20
Chiv. 21:8Miy 10:7; Ahe 10:26; Chv 2:11; 20:6
Chiv. 21:9Le 26:21; Chv 15:1
Chiv. 21:9Sl 45:9; Chv 19:7
Chiv. 21:10Yes 2:2; Eze 40:2; Mik 4:1
Chiv. 21:10Yes 52:1
Chiv. 21:10Ahe 12:22; Chv 3:12; 21:2
Chiv. 21:11Yes 60:1
Chiv. 21:11Eks 24:10
Chiv. 21:12Yes 60:18
Chiv. 21:12Eks 28:21; 39:14
Chiv. 21:13Chv 22:14
Chiv. 21:14Ahe 11:10
Chiv. 21:14Mt 10:2; Lu 6:13; Mac 1:13; Aef 2:20
Chiv. 21:15Eze 40:3; Chv 11:1
Chiv. 21:15Eze 40:5
Chiv. 21:16Chv 3:12
Chiv. 21:18Chv 4:3; 21:11
Chiv. 21:19Yes 54:11
Chiv. 21:19Yes 54:12
Chiv. 21:19Eks 28:18; Eze 28:13
Chiv. 21:19Eks 39:11; Yob 28:6
Chiv. 21:19Eks 28:17; Chv 4:3
Chiv. 21:20Eks 28:20; Nym 5:14; Eze 1:16; Da 10:6
Chiv. 21:20Eks 28:17; 39:10; Yob 28:19; Eze 28:13
Chiv. 21:20Eks 28:19; 39:12
Chiv. 21:21Est 1:6; Yob 28:18; Mt 13:46
Chiv. 21:22Mac 7:49
Chiv. 21:22Sl 11:4
Chiv. 21:22Eks 6:3; Chv 15:3
Chiv. 21:22Yoh 4:23
Chiv. 21:22Aef 2:20
Chiv. 21:23Yes 60:19; Chv 22:5
Chiv. 21:23Yoh 1:9; Mac 26:13; Ahe 1:3
Chiv. 21:24Yes 60:3
Chiv. 21:24Sl 138:4
Chiv. 21:25Yes 60:11
Chiv. 21:25Yes 60:20
Chiv. 21:26Yes 60:5
Chiv. 21:271Ak 6:9; Aga 5:21
Chiv. 21:27Sl 5:6; Akl 3:9; Chv 21:8
Chiv. 21:27Yes 52:1
Chiv. 21:27Da 12:1; Afi 4:3; Chv 13:8
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 21:1-27

Chivumbulutso

21 Tsopano ndinaona kumwamba+ kwatsopano ndi dziko lapansi+ latsopano, pakuti kumwamba+ kwakale ndi dziko lapansi lakale+ zinali zitachoka, ndipo kulibenso nyanja.+ 2 Ndinaonanso mzinda woyera,+ Yerusalemu Watsopano, ukutsika kuchokera kumwamba+ kwa Mulungu, utakonzedwa ngati mkwatibwi+ wokongoletsedwera mwamuna wake.+ 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Taonani! Chihema+ cha Mulungu chili pakati pa anthu. Iye adzakhala pamodzi nawo,+ ndipo iwo adzakhala anthu ake.+ Zoonadi, Mulunguyo adzakhala nawo.+ 4 Iye adzapukuta misozi+ yonse m’maso mwawo, ndipo imfa sidzakhalaponso.+ Sipadzakhalanso kulira,+ kapena kubuula, ngakhale kupweteka. Zakalezo zapita.”+

5 Ndipo wokhala pampando wachifumu+ anati: “Taonani! Zinthu zonse zimene ndikupanga n’zatsopano.”+ Ananenanso kuti: “Lemba, pakuti mawu awa ndi odalirika ndi oona.” 6 Anandiuzanso kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega, chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense womva ludzu, ndidzamupatsa madzi a m’kasupe wa moyo kwaulere.+ 7 Aliyense wopambana pa nkhondo adzalandira zimenezi monga cholowa. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake,+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ 8 Koma amantha, opanda chikhulupiriro,+ odetsedwa amenenso amachita zinthu zonyansa,+ opha anthu,+ adama,+ ochita zamizimu, opembedza mafano,+ ndi onse abodza,+ gawo lawo lidzakhala m’nyanja yoyaka moto+ ndi sulufule.+ Nyanja imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.”+

9 Ndipo kunabwera mmodzi wa angelo 7 aja, amene anali ndi mbale 7 zodzaza ndi miliri+ 7 yotsiriza. Iye anandiuza kuti: “Bwera kuno ndikuonetse mkwatibwi, mkazi wa Mwanawankhosa.”+ 10 Choncho, mu mphamvu ya mzimu, ananditengera kuphiri lalikulu ndi lalitali,+ ndipo anandionetsa mzinda woyera,+ Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+ 11 uli ndi ulemerero wa Mulungu.+ Unali wonyezimira ngati mwala wamtengo wapatali kwambiri, ngati mwala wa yasipi wowala mbee! ngati galasi.+ 12 Mzindawo unali ndi mpanda waukulu ndi wautali,+ ndipo unali ndi zipata 12. Pazipatazo panali angelo 12, ndipo panalembedwa mayina a mafuko 12 a ana a Isiraeli.+ 13 Kum’mawa kwa mzindawo kunali zipata zitatu, kumpoto zipata zitatu, kum’mwera zipata zitatu, ndipo kumadzulo kwake zipata zitatu.+ 14 Mpanda wa mzindawo unalinso ndi miyala yomangira maziko+ yokwana 12, ndipo pamiyalayo panali mayina 12 a atumwi 12+ a Mwanawankhosa.

15 Tsopano amene anali kundilankhula uja ananyamula bango+ lagolide loyezera, kuti ayeze mzindawo, zipata zake, ndi mpanda wake.+ 16 Mzindawo unali ndi mbali zinayi zofanana kutalika kwake. M’litali mwake n’chimodzimodzi ndi m’lifupi mwake. Mngeloyo anayeza mzindawo+ ndi bangolo, ndipo anapeza kuti unali masitadiya 12,000* kuuzungulira. M’litali mwake, m’lifupi mwake, ndi msinkhu wake, n’zofanana. 17 Anayezanso mpanda wake, ndipo unali wautali mikono 144,* malinga ndi muyezo wa munthu, umene ulinso wofanana ndi muyezo wa mngelo. 18 Mpandawo unali womangidwa ndi mwala wa yasipi,+ ndipo mzindawo unali womangidwa ndi golide woyenga bwino woonekera ngati galasi. 19 Maziko+ a mpanda wa mzindawo anawakongoletsa ndi miyala yamtengo wapatali ya mitundu yonse:+ maziko oyamba anali amwala wa yasipi,+ achiwiri wa safiro,+ achitatu wa kalikedo, achinayi wa emarodi,+ 20 achisanu wa sadonu, a 6 wa sadiyo, a 7 wa kulusolito,+ a 8 wa belulo, a 9 wa topazi,+ a 10 wa kulusopurazo, a 11 wa huwakinto, ndipo a 12, wa ametusito.*+ 21 Komanso zitseko za pazipata 12 zija zinali ngale 12. Chitseko chilichonse chinali ngale imodzi.+ Ndipo msewu waukulu wa mumzindawo unali wopangidwa ndi golide woyenga bwino woonekera ngati galasi.

22 Sindinaone kachisi mumzindawo,+ pakuti Yehova+ Mulungu Wamphamvuyonse+ ndiye anali kachisi+ wake, komanso Mwanawankhosa ndiye kachisi wake.+ 23 Mzindawo sunafunikirenso kuwala kwa dzuwa kapena kwa mwezi, pakuti ulemerero wa Mulungu unauwalitsa,+ ndipo nyale yake inali Mwanawankhosa.+ 24 Mitundu ya anthu idzayenda mwa kuwala kwake,+ ndipo mafumu a dziko lapansi adzabweretsa ulemerero wawo mumzindawo.+ 25 Zipata zake sizidzatsekedwa n’komwe masana,+ ndipo usiku sudzakhalako.+ 26 Iwo adzabweretsa ulemerero ndi ulemu wa mitundu ya anthu mumzindawo.+ 27 Koma chilichonse chosapatulika, ndi aliyense wochita zonyansa+ ndiponso wabodza,+ sadzalowa mumzindawo.+ Amene adzalowemo ndi okhawo olembedwa mumpukutu wa moyo, umene ndi wa Mwanawankhosa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena