Numeri 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aroni ndi ana ake amveketse dzina langa+ pakati pa ana a Isiraeli kuti ndiwadalitse.”+ 2 Mbiri 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo anthu anga+ otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa+ n’kupemphera,+ n’kufunafuna nkhope yanga,+ n’kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba+ n’kuwakhululukira tchimo lawo+ ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+ Yesaya 43:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Inu ndinu mboni zanga,”+ akutero Yehova. “Ndinu mtumiki wanga amene ndakusankhani+ kuti mundidziwe+ ndi kundikhulupirira,+ komanso kuti mumvetse kuti ine sindinasinthe.+ Ine ndisanakhaleko kunalibe Mulungu amene anapangidwa,+ ndipo pambuyo panga palibenso wina.+ Yesaya 63:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kwanthawi yaitali, takhala ngati anthu amene simunawalamulirepo, ngati anthu amene sanatchedwepo ndi dzina lanu.+ Danieli 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Imvani, inu Yehova.+ Tikhululukireni, inu Yehova.+ Timvereni ndipo muchitepo kanthu,+ inu Yehova. Inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu musazengereze,+ pakuti mzinda wanu ndi anthu anu amatchedwa ndi dzina lanu.”+ Machitidwe 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachita zimenezi kuti anthu otsalirawo afunefune Yehova ndi mtima wonse. Amufunefune pamodzi ndi mitundu yonse ya anthu, anthu otchedwa ndi dzina langa, watero Yehova amene akuchita zinthu zimenezi,+
14 ndipo anthu anga+ otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa+ n’kupemphera,+ n’kufunafuna nkhope yanga,+ n’kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba+ n’kuwakhululukira tchimo lawo+ ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+
10 “Inu ndinu mboni zanga,”+ akutero Yehova. “Ndinu mtumiki wanga amene ndakusankhani+ kuti mundidziwe+ ndi kundikhulupirira,+ komanso kuti mumvetse kuti ine sindinasinthe.+ Ine ndisanakhaleko kunalibe Mulungu amene anapangidwa,+ ndipo pambuyo panga palibenso wina.+
19 Kwanthawi yaitali, takhala ngati anthu amene simunawalamulirepo, ngati anthu amene sanatchedwepo ndi dzina lanu.+
19 Imvani, inu Yehova.+ Tikhululukireni, inu Yehova.+ Timvereni ndipo muchitepo kanthu,+ inu Yehova. Inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu musazengereze,+ pakuti mzinda wanu ndi anthu anu amatchedwa ndi dzina lanu.”+
17 Ndidzachita zimenezi kuti anthu otsalirawo afunefune Yehova ndi mtima wonse. Amufunefune pamodzi ndi mitundu yonse ya anthu, anthu otchedwa ndi dzina langa, watero Yehova amene akuchita zinthu zimenezi,+