Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Usalandire chiphuphu chifukwa chiphuphu chimachititsa khungu anthu amaso akuthwa, ndipo chingapotoze mawu a anthu olungama.+

  • Numeri 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndithu ndidzakupatsani ulemerero waukulu,+ ndipo chilichonse chimene mungandiuze ndidzachita.+ Chonde tabwerani mudzanditembererere anthuwa.’”

  • Oweruza 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Delila ataona kuti Samisoni wamuululira zonse za pansi pa mtima wake, nthawi yomweyo anatumiza mthenga kukaitana olamulira ogwirizana a Afilisiti,+ kuti: “Bwerani tsopano popeza wandiululira zonse za pansi pa mtima wake.”+ Pamenepo olamulira ogwirizana a Afilisiti aja anabwera kwa Delila ndipo anam’patsa ndalama.+

  • Miyambo 17:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Woipa amatenga chiphuphu mobisa,+ kuti akhotetse njira za chiweruzo.+

  • Mlaliki 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kuponderezedwa kumapangitsa munthu wanzeru kuchita zinthu zopanda nzeru,+ ndipo mphatso+ ikhoza kuwononga mtima wa munthu.+

  • Mateyu 26:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 n’kuwafunsa kuti: “Kodi mudzandipatsa chiyani ndikamupereka kwa inu?”+ Iwo anamulonjeza ndalama 30 zasiliva.+

  • 1 Timoteyo 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti kukonda+ ndalama ndi muzu+ wa zopweteka za mtundu uliwonse,+ ndipo pokulitsa chikondi chimenechi, ena asocheretsedwa n’kusiya chikhulupiriro ndipo adzibweretsera zopweteka zambiri pathupi lawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena