Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 14:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Koma anthu anauza Sauli kuti: “Kodi Yonatani amene wagwira ntchito yobweretsa chipulumutso chachikulu chimenechi+ mu Isiraeli afe? Sizitheka zimenezo!+ Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ ngakhale tsitsi limodzi+ la m’mutu wake siligwa pansi, pakuti iye wachita zimenezi lero mothandizidwa ndi Mulungu.”+ Ndi mawu amenewa anthuwo anapulumutsa+ Yonatani, moti sanafe.

  • 1 Samueli 18:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula ndi Sauli, Yonatani+ anagwirizana kwambiri+ ndi Davide, moti anayamba kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera yekha.+

  • 2 Samueli 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Sauli ndi Yonatani,+ anthu okondeka ndi osangalatsa pamene anali ndi moyo,

      Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+

      Iwo anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+

      Amphamvu kuposa mikango.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena