Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 31:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Mulungu wa bambo anga,+ Mulungu wa Abulahamu, Mulungu amene Isaki anali kumuopa,+ akanapanda kukhala kumbali yanga, bwenzi mutandibweza kwathu chimanjamanja. Koma Mulungu waona kusautsika kwanga ndi ntchito zimene ndagwira molimbika, n’chifukwa chake anakudzudzulani usiku wapitawu.”+

  • 1 Samueli 26:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehova adzabwezera aliyense malinga ndi chilungamo+ ndi kukhulupirika kwake, pakuti lero Yehova anakuperekani m’manja mwanga, koma sindinafune kutambasula dzanja langa ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+

  • Salimo 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Nyamukani, inu Yehova, mu mkwiyo wanu.+

      Imirirani ndi kukhaulitsa amene andisonyeza mkwiyo ndi kundichitira zoipa.+

      Dzukani ndi kundithandiza,+ pakuti mwalamula kuti chiweruzo chiperekedwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena