Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 kufikira ine nditabwera kudzakutengerani kudziko lofanana ndi dziko lanulo+ kuti mukhalebe ndi moyo osafa. Ndidzakutengerani kudziko la mbewu ndi la vinyo watsopano, dziko la mkate+ ndi minda ya mpesa,+ dziko la mitengo ya maolivi a mafuta ndiponso la uchi.+ Musamvere Hezekiya chifukwa akukunyengererani ndi mawu akuti, ‘Yehova atilanditsa.’+

  • 2 Mbiri 32:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 lye analembanso makalata+ onyoza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ komanso omutonza kuti: “Mofanana ndi milungu+ ya mitundu ya mayiko ena imene sinapulumutse anthu ake m’manja mwanga,+ Mulungu wa Hezekiya sapulumutsa anthu ake m’manja mwanga.”

  • Yesaya 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Yehova akadzatsiriza ntchito yake yonse m’phiri la Ziyoni ndi mu Yerusalemu, ndidzalanga mfumu ya Asuri chifukwa cha zipatso za mwano wa mumtima mwake ndiponso chifukwa cha kudzikuza kwa maso ake onyada.+

  • Yesaya 36:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Musamvere Hezekiya chifukwa akukunyengererani+ ndi mawu akuti, ‘Yehova atilanditsa.’ Kodi pali mulungu wa mitundu ina amene wakwanitsa kupulumutsa mtundu wake m’manja mwa mfumu ya Asuri?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena