Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 36:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Tenga mpukutu+ ndi kulembamo mawu onse+ amene ndakuuza okhudza chilango chimene ndidzapatsa Isiraeli, Yuda+ ndi mitundu yonse ya anthu.+ Ulembe mawu onse amene ndakuuza kuchokera nthawi imene ndinalankhula nawe m’masiku a Yosiya kufikira lero.+

  • Yeremiya 51:60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 60 Yeremiya analemba m’buku limodzi+ za masoka onse odzagwera Babulo. Iye analemba mawu onsewa okhudza zimene zidzachitikire Babulo.

  • Danieli 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 M’chaka choyamba cha ulamuliro wa Belisazara+ mfumu ya Babulo, Danieli analota maloto ndipo anaona masomphenya atagona pabedi lake.+ Pa nthawi imeneyo, analemba zimene analotazo,+ ndipo anafotokoza nkhani yonseyo.

  • Habakuku 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo Yehova anandiyankha kuti: “Lemba masomphenyawa moonekera bwino pamiyala yosema,+ kuti wowerenga mokweza awerenge mosadodoma.+

  • Aroma 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Zinthu zonse zimene zinalembedwa+ kalekale zinalembedwa kuti zitilangize.+ Malembawa amatipatsa chiyembekezo+ chifukwa amatithandiza kupirira+ ndiponso amatilimbikitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena