Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “Ndiyeno zikadzachitika kuti mawu onsewa akwaniritsidwa pa inu, madalitso+ ndi matemberero+ amene ndakuikirani pamaso panu, ndipo mwakumbukira mawu amenewa mumtima mwanu+ muli pakati pa mitundu yonse kumene Yehova Mulungu wanu adzakubalalitsirani,+

  • Salimo 137:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 137 Tinakhala pansi+ m’mphepete mwa mitsinje ya ku Babulo,+

      Ndipo tinalira titakumbukira Ziyoni.+

  • Ezekieli 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakati pawo ndidzapulumutsapo amuna ochepa kuti asaphedwe ndi lupanga,+ njala, kapena miliri, n’cholinga chakuti akafotokoze za zinthu zawo zonse zonyansa+ pakati pa mitundu imene akakhaleko,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”

  • Zekariya 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndidzawamwaza ngati mbewu pakati pa anthu a mitundu ina+ ndipo adzandikumbukira ali kumadera akutali.+ Iwowo ndi ana awo adzapezanso mphamvu ndipo adzabwerera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena