2 Mafumu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Puli+ mfumu ya Asuri+ inabwera m’dzikomo. Choncho Menahemu anapatsa+ Puli matalente* 1,000 a siliva,+ kuti amuthandize kulimbitsa ufumu umene unali m’manja mwake.+ Ezekieli 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Anali kulakalaka kwambiri amuna amene ankakhumba kugona naye.+ Anali kulakalaka Asuri+ amene anali kukhala moyandikana naye. Hoseya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Efuraimu anaona kudwala kwake ndipo Yuda anaona chilonda chake.+ Pamenepo Efuraimu anapita ku Asuri+ ndipo anatumiza amithenga kwa mfumu yaikulu.+ Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani anthu inu,+ ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.+ Hoseya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Efuraimu akudya mphepo+ ndi kuthamangitsa mphepo ya kum’mawa tsiku lonse.+ Iye akuchulukitsa mabodza ndipo akuwononga zinthu zambiri.+ Wachita pangano ndi Asuri+ ndipo wapititsa mafuta ku Iguputo.
19 Tsopano Puli+ mfumu ya Asuri+ inabwera m’dzikomo. Choncho Menahemu anapatsa+ Puli matalente* 1,000 a siliva,+ kuti amuthandize kulimbitsa ufumu umene unali m’manja mwake.+
5 “Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Anali kulakalaka kwambiri amuna amene ankakhumba kugona naye.+ Anali kulakalaka Asuri+ amene anali kukhala moyandikana naye.
13 “Efuraimu anaona kudwala kwake ndipo Yuda anaona chilonda chake.+ Pamenepo Efuraimu anapita ku Asuri+ ndipo anatumiza amithenga kwa mfumu yaikulu.+ Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani anthu inu,+ ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.+
12 “Efuraimu akudya mphepo+ ndi kuthamangitsa mphepo ya kum’mawa tsiku lonse.+ Iye akuchulukitsa mabodza ndipo akuwononga zinthu zambiri.+ Wachita pangano ndi Asuri+ ndipo wapititsa mafuta ku Iguputo.