Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+

  • Yohane 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Pa chiyambi,+ panali wina wotchedwa Mawu,+ ndipo Mawuyo anali ndi Mulungu,+ komanso Mawuyo anali mulungu.*+

  • Yohane 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+

  • Yohane 14:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Mwandimva ndikukuuzani kuti, Ndikupita ndipo ndidzabweranso kwa inu. Ngati munali kundikonda, mukanakondwera kuti ndikupita kwa Atate wanga, chifukwa Atate ndi wamkulu+ kuposa ine.

  • Yohane 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Yesu anati: “Usandikangamire. Pakuti sindinakwerebe kwa Atate. Koma pita kwa abale anga+ ukawauze kuti, ‘Ine ndikukwera kwa Atate+ wanga ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”+

  • Yohane 20:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Koma izi zalembedwa+ kuti mukhulupirire kuti Yesu alidi Khristu Mwana wa Mulungu, ndi kutinso, mwa kukhulupirira,+ mukhale ndi moyo m’dzina lake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena