Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 19
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 19:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “Aleluya.” Onani mawu a m’munsi pa Eks 15:2.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:10
  • +Sl 150:6
  • +Chv 12:10
  • +Chv 7:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 272

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, tsa. 16

Chivumbulutso 19:2

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 7.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 32:4; Sl 19:9; 1Pe 1:17; Chv 15:3
  • +De 32:43; 2Mf 9:7; Sl 79:10; Chv 18:20, 24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 272

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, tsa. 16

Chivumbulutso 19:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 117:1
  • +Yes 34:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 272-273

Chivumbulutso 19:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:4
  • +Chv 4:6
  • +1Mf 22:19; Yes 6:1
  • +Sl 106:48

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 273-274

Chivumbulutso 19:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 134:1; 135:1
  • +Sl 115:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 274

Chivumbulutso 19:6

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 2.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 113:1
  • +Eks 6:3
  • +Sl 97:1; Yes 52:7; Da 7:9; Chv 11:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 274-275

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1993, ptsa. 25-26

    12/15/1990, tsa. 16

    7/1/1989, ptsa. 23-24

Chivumbulutso 19:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 7:12
  • +Mt 25:10; Chv 19:9
  • +1At 4:16
  • +2Ak 11:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2014, tsa. 22

    2/15/2014, ptsa. 8-12

    7/1/1995, ptsa. 13-14

    5/1/1993, tsa. 26

    8/15/1990, tsa. 31

    8/15/1989, tsa. 29

    7/1/1989, ptsa. 23-24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 276-277

Chivumbulutso 19:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 61:10; Aef 5:27; Chv 14:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 276

Chivumbulutso 19:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 22:3; Lu 14:17
  • +Lu 14:15
  • +Yoh 3:34; 8:47

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 19

    2/15/2014, ptsa. 10-11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 72, 277-278

Chivumbulutso 19:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 22:8
  • +Mac 10:26; Chv 22:9
  • +Mt 28:19; Mac 1:8
  • +Mt 4:10; Yoh 4:23
  • +Lu 24:27; Mac 2:17; 10:43; 1Pe 1:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2009, tsa. 5

    5/1/1987, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 278-279

Chivumbulutso 19:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yob 39:25; Miy 21:31; Yer 8:6; Chv 6:2
  • +Ahe 3:6; Chv 1:5
  • +Yoh 1:14; Chv 3:14
  • +Yes 11:4; Ahe 1:8, 9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 17

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 280

Chivumbulutso 19:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:14; 2:18
  • +Chv 19:16
  • +Chv 2:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 65, 280-281

Chivumbulutso 19:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 12:24; 1Pe 1:2
  • +Yoh 1:1; 1Yo 1:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 281

Chivumbulutso 19:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 17

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2014, ptsa. 6-7

    2/15/2009, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 281

Chivumbulutso 19:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2At 2:8; Chv 1:16
  • +Sl 2:9; Chv 2:27; 12:5
  • +Yer 25:30; Yow 3:13; Chv 14:20
  • +Chv 14:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 282-284

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1990, ptsa. 4-5

Chivumbulutso 19:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 28:18; Afi 2:10; 1Ti 6:15; Chv 17:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 284

Chivumbulutso 19:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Sa 17:46; Eze 39:4, 17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 284-285

Chivumbulutso 19:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 39:17
  • +Eze 39:18
  • +Eze 39:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 13, 284-285

Chivumbulutso 19:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:1
  • +Chv 16:14; 17:12
  • +Eze 38:16; Chv 16:16
  • +Sl 2:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2020, tsa. 15

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2015, tsa. 29

    3/15/2007, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 285-286

Chivumbulutso 19:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:18
  • +Chv 13:11; 16:13
  • +Chv 13:13
  • +Chv 13:16
  • +Chv 13:15
  • +Mt 10:28; 2Pe 2:6; Yuda 7; Chv 20:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 11

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2148

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 285-286

Chivumbulutso 19:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:2
  • +Chv 2:16
  • +Eze 39:4; Chv 19:17
  • +Eze 39:20
  • +Eze 39:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 285-286

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 19:1Da 7:10
Chiv. 19:1Sl 150:6
Chiv. 19:1Chv 12:10
Chiv. 19:1Chv 7:12
Chiv. 19:2De 32:4; Sl 19:9; 1Pe 1:17; Chv 15:3
Chiv. 19:2De 32:43; 2Mf 9:7; Sl 79:10; Chv 18:20, 24
Chiv. 19:3Sl 117:1
Chiv. 19:3Yes 34:10
Chiv. 19:4Chv 4:4
Chiv. 19:4Chv 4:6
Chiv. 19:41Mf 22:19; Yes 6:1
Chiv. 19:4Sl 106:48
Chiv. 19:5Sl 134:1; 135:1
Chiv. 19:5Sl 115:13
Chiv. 19:6Sl 113:1
Chiv. 19:6Eks 6:3
Chiv. 19:6Sl 97:1; Yes 52:7; Da 7:9; Chv 11:15
Chiv. 19:7Chv 7:12
Chiv. 19:7Mt 25:10; Chv 19:9
Chiv. 19:71At 4:16
Chiv. 19:72Ak 11:2
Chiv. 19:8Yes 61:10; Aef 5:27; Chv 14:4
Chiv. 19:9Mt 22:3; Lu 14:17
Chiv. 19:9Lu 14:15
Chiv. 19:9Yoh 3:34; 8:47
Chiv. 19:10Chv 22:8
Chiv. 19:10Mac 10:26; Chv 22:9
Chiv. 19:10Mt 28:19; Mac 1:8
Chiv. 19:10Mt 4:10; Yoh 4:23
Chiv. 19:10Lu 24:27; Mac 2:17; 10:43; 1Pe 1:11
Chiv. 19:11Yob 39:25; Miy 21:31; Yer 8:6; Chv 6:2
Chiv. 19:11Ahe 3:6; Chv 1:5
Chiv. 19:11Yoh 1:14; Chv 3:14
Chiv. 19:11Yes 11:4; Ahe 1:8, 9
Chiv. 19:12Chv 1:14; 2:18
Chiv. 19:12Chv 19:16
Chiv. 19:12Chv 2:17
Chiv. 19:13Ahe 12:24; 1Pe 1:2
Chiv. 19:13Yoh 1:1; 1Yo 1:1
Chiv. 19:152At 2:8; Chv 1:16
Chiv. 19:15Sl 2:9; Chv 2:27; 12:5
Chiv. 19:15Yer 25:30; Yow 3:13; Chv 14:20
Chiv. 19:15Chv 14:19
Chiv. 19:16Mt 28:18; Afi 2:10; 1Ti 6:15; Chv 17:14
Chiv. 19:171Sa 17:46; Eze 39:4, 17
Chiv. 19:18Eze 39:17
Chiv. 19:18Eze 39:18
Chiv. 19:18Eze 39:20
Chiv. 19:19Chv 13:1
Chiv. 19:19Chv 16:14; 17:12
Chiv. 19:19Eze 38:16; Chv 16:16
Chiv. 19:19Sl 2:2
Chiv. 19:20Chv 13:18
Chiv. 19:20Chv 13:11; 16:13
Chiv. 19:20Chv 13:13
Chiv. 19:20Chv 13:16
Chiv. 19:20Chv 13:15
Chiv. 19:20Mt 10:28; 2Pe 2:6; Yuda 7; Chv 20:14
Chiv. 19:21Chv 6:2
Chiv. 19:21Chv 2:16
Chiv. 19:21Eze 39:4; Chv 19:17
Chiv. 19:21Eze 39:20
Chiv. 19:21Eze 39:17
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 19:1-21

Chivumbulutso

19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+ 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+ 3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya, anthu inu!+ Utsi wochokera kwa iye udzafuka kwamuyaya.”+

4 Ndipo akulu+ 24 ndi zamoyo zinayi zija,+ anagwada pansi ndi kuwerama, n’kulambira Mulungu wokhala+ pampando wachifumu, ndi mawu akuti: “Ame! Tamandani Ya,+ anthu inu!”

5 Komanso, kunamveka mawu ochokera kumpando wachifumu akuti: “Muzitamanda Mulungu wathu, inu nonse akapolo+ ake, inu omuopa, olemekezeka ndi onyozeka omwe.”+

6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+ 7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya. Timupatse ulemerero,+ chifukwa ukwati+ wa Mwanawankhosa wafika,+ ndipo mkazi wake wadzikongoletsa.+ 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+

9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+ 10 Pamenepo ndinagwada pansi n’kuwerama patsogolo pa mapazi ake kuti ndimulambire.+ Koma iye anandiuza kuti:+ “Samala! Usatero ayi! Inetu ndangokhala kapolo mnzako, ndi wa abale ako amene ali ndi ntchito yochitira umboni za Yesu.+ Lambira Mulungu,+ pakuti kuchitira umboni za Yesu ndiko cholinga cha maulosi.”+

11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+ 12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu+ zambiri. Anali ndi dzina+ lolembedwa limene wina aliyense sanali kulidziwa, koma iye yekha. 13 Iye anavala malaya akunja owazidwa magazi,+ ndipo dzina limene anali kutchedwa nalo linali lakuti Mawu+ a Mulungu. 14 Komanso magulu ankhondo amene anali kumwamba, anali kumutsatira pamahatchi oyera, atavala zovala zapamwamba, zoyera bwino, za mbee! 15 M’kamwa mwake munali kutuluka lupanga+ lalitali lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu, ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Iye anali kupondapondanso m’chopondera mphesa+ cha mkwiyo waukulu wa Mulungu+ Wamphamvuyonse. 16 Pamalaya ake akunja, ngakhale pantchafu yake, anali ndi dzina lolembedwa lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+

17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo, 18 kuti mudzadye minofu+ ya mafumu, ya akuluakulu a asilikali, ya amuna amphamvu,+ ya mahatchi+ ndi ya okwerapo ake, ndi minofu ya onse, ya mfulu ndi ya akapolo, ya olemekezeka ndi ya onyozeka.”

19 Ndipo ndinaona chilombo,+ mafumu+ a dziko lapansi, ndi magulu awo ankhondo atasonkhana pamodzi kuti amenyane+ ndi wokwera pahatchi+ uja ndi gulu lake lankhondo. 20 Koma chilombocho+ chinagwidwa limodzi ndi mneneri+ wonyenga uja, amene anachita zizindikiro+ pamaso pa chilombocho. Zizindikiro zimenezi anasocheretsa nazo olandira chizindikiro+ cha chilombo ndi olambira chifaniziro chake.+ Adakali amoyo, onse awiri anaponyedwa m’nyanja ya moto yoyaka ndi sulufule.+ 21 Koma ena onse anaphedwa ndi lupanga lalitali la wokwera pahatchi,+ limene linatuluka m’kamwa mwake lija.+ Ndipo mbalame+ zonse zinakhuta+ minofu yawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena