Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma mwa anthu onsewa, usankhe amuna oyenerera,+ oopa Mulungu,+ okhulupirika,+ odana ndi kupeza phindu mwachinyengo.+ Amenewa uwaike kukhala otsogolera anthuwa, ndipo pakhale atsogoleri a magulu a anthu 1,000,+ atsogoleri a magulu a anthu 100, atsogoleri a magulu a anthu 50 ndi atsogoleri a magulu a anthu 10.+

  • Numeri 16:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo anaukira Mose. Oukirawo anali limodzi ndi amuna achiisiraeli okwanira 250. Iwowa anali atsogoleri a anthuwo, owaimira kumisonkhano, amuna otchuka.

  • Numeri 34:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Musankhe mtsogoleri mmodzi pa fuko lililonse, kuti akathandize kugawa cholowa cha malo.+

  • Yoswa 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anam’tumiza pamodzi ndi atsogoleri 10. Fuko lililonse la Isiraeli linatumiza mtsogoleri mmodzi woimira nyumba ya makolo ake. Mtsogoleri aliyense anali woimira nyumba ya bambo ake pakati pa Aisiraeli masauzande.+

  • 2 Samueli 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Davide atawerengadi anthuwo anavutika mumtima mwake.+ Choncho Davide anauza Yehova kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimene ndachitazi. Tsopano Yehova, khululukani cholakwa cha ine mtumiki wanu+ chonde, pakuti ndachita chinthu chopusa kwambiri.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena