-
Yoswa 10:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Tsopano Adoni-zedeki, mfumu ya Yerusalemu anamva zakuti Yoswa walanda mzinda wa Ai+ ndi kuuwononga.+ Iye anamva kuti Yoswa wawononga mzindawo ndi kupha mfumu yake+ monga anachitira ndi mzinda wa Yeriko+ ndi mfumu yake.+ Anamvanso kuti anthu okhala ku Gibeoni apangana za mtendere ndi Aisiraeli+ ndipo akukhala pakati pawo. Atangomva zimenezi,
-