Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 “Yamikani Yehova,+ anthu inu. Itanani pa dzina lake.+

      Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake!+

  • 2 Mbiri 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano anthu oimba malipenga ndi oimba pakamwa anayamba kuimba mogwirizana+ n’kumamveka ngati mawu amodzi otamanda ndi kuthokoza Yehova. Komanso anayamba kuimba+ ndi malipenga, zinganga, ndi zoimbira zina potamanda+ Yehova ndi mawu akuti, “chifukwa iye ndi wabwino,+ pakuti kukoma mtima kwake kosatha+ kudzakhala mpaka kalekale.” Kenako mtambo unadzaza nyumbayo,+ nyumba ya Yehova.+

  • Ezara 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo anayamba kuimba molandizana potamanda+ ndi kuthokoza Yehova kuti, “iye ndi wabwino,+ pakuti kukoma mtima kosatha kumene amakusonyeza kwa Isiraeli kudzakhala mpaka kalekale.”*+ Ndipo anthu onse anafuula mokweza kwambiri+ potamanda Yehova chifukwa cha kumangidwa kwa maziko a nyumba ya Yehova.

  • Salimo 89:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Pakuti ndanena kuti: “Kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhazikika mpaka kalekale.+

      Ndipo mwakhazikitsa kukhulupirika kwanu kumwamba.”+

  • Yesaya 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+

  • Mika 7:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena