Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno amuna ena ochokera ku Yudeya+ anapita kumeneko ndi kuyamba kuphunzitsa abale kuti: “Mukapanda kudulidwa+ malinga ndi mwambo wa Mose,+ simungapulumuke.”

  • Machitidwe 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Inetu ndine Myuda,+ wobadwira ku Tariso wa ku Kilikiya,+ koma ndinaphunzitsidwa ndi Gamaliyeli+ mumzinda womwe uno. Anandiphunzitsa kutsatira Chilamulo cha makolo athu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+ Ndipo ndinali wodzipereka+ potumikira Mulungu monga mmene nonsenu mulili lero.

  • Aroma 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti ndikuwachitira umboni kuti ndi odzipereka+ potumikira Mulungu, koma samudziwa molondola.+

  • Agalatiya 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndinali kupita patsogolo kwambiri m’Chiyuda kuposa anzanga ambiri a fuko langa, omwe anali amsinkhu wanga.+ Pakuti ndinali wodzipereka kwambiri+ pa miyambo+ ya makolo anga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena