Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘Usalole kuti aliyense mwa ana ako aperekedwe+ kwa Moleki.*+ Usanyoze+ dzina la Mulungu wako mwa njira imeneyi. Ine ndine Yehova.+

  • Levitiko 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ine ndidzam’kana* munthu ameneyo, ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki kuti aipitse malo anga oyera+ ndi kuipitsa dzina langa loyera.+

  • Deuteronomo 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 moti akupita kukalambira milungu ina ndi kuigwadira, kapena kugwadira dzuwa, mwezi kapena khamu lonse la zinthu zakuthambo,+ chinthu chimene ine sindinakulamuleni,+

  • Yeremiya 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iwo amangiranso Baala malo okwezeka kuti azitentherapo ana awo aamuna monga nsembe zopsereza zathunthu zoperekedwa kwa Baala.+ Ine sindinawalamule zimenezi kapena kuzitchula,+ ndipo sindinaziganizirepo mumtima mwanga.”’+

  • Yeremiya 32:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Kuwonjezera apo anamangira Baala+ malo okwezeka m’chigwa cha mwana wa Hinomu.+ Anachita izi kuti azidutsitsa ana awo aamuna ndi ana awo aakazi pamoto monga nsembe+ kwa Moleki.+ Ine sindinawalamule zimenezi+ ndipo sindinaganizirepo mumtima mwanga kuchita chinthu chonyansa chimenechi,+ kuti Yuda achite tchimo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena