Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 22
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Mtsinje wa madzi amoyo (1-5)

      • Mawu omaliza (6-21)

        • ‘Bwerani! Mudzamwe madzi opatsa moyo kwaulere’ (17)

        • “Bwerani, Ambuye Yesu” (20)

Chivumbulutso 22:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 47:1
  • +Yoh 1:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 30

    2/15/2009, tsa. 5

    6/1/2008, ptsa. 14-15

    9/15/2002, tsa. 32

    3/1/1999, tsa. 22

    9/15/1991, ptsa. 18-19

    12/15/1990, ptsa. 10-11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 310-311

Chivumbulutso 22:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 47:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2015, tsa. 27

    1/15/2012, tsa. 30

    3/1/1999, tsa. 22

    11/1/1992, tsa. 7

    9/15/1991, ptsa. 18-19

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 310-312

Chivumbulutso 22:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 312-313

Chivumbulutso 22:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 5:8
  • +Chv 14:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 312-313

Chivumbulutso 22:5

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 21:25
  • +Yes 60:19, 20; 1Yo 1:5
  • +Da 7:18; Chv 3:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 313

Chivumbulutso 22:6

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Tit 1:2
  • +2Ti 3:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, tsa. 19

Chivumbulutso 22:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:15; 22:20
  • +Yoh 13:17; Chv 1:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 6, 314

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, tsa. 19

Chivumbulutso 22:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314

    Nsanja ya Olonda,

    8/1/1999, tsa. 14

Chivumbulutso 22:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 4:10; Mac 10:25, 26; Chv 19:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314

    Nsanja ya Olonda,

    8/1/1999, tsa. 14

Chivumbulutso 22:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 315

Chivumbulutso 22:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 315-316

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1999, tsa. 7

Chivumbulutso 22:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 62:12; Yes 40:10; Aro 2:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317

    Kukambitsirana, tsa. 399

Chivumbulutso 22:13

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “ndine A ndi Z.” Alefa ndi chilembo choyambirira cha afabeti ya Chigiriki ndipo Omega ndi chilembo chomalizira.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 44:6; 48:12; Chv 1:8; 21:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317

    Kukambitsirana, tsa. 399

Chivumbulutso 22:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 1:7
  • +Chv 2:7
  • +Chv 21:10, 12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2018, tsa. 20

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317

Chivumbulutso 22:15

Mawu a M'munsi

  • *

    Amenewa ndi anthu amene zochita zawo ndi zonyansa pamaso pa Mulungu.

  • *

    Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 5:19-21; Aef 5:5; Chv 21:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 316-317

Chivumbulutso 22:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 11:1, 10; 53:2; Yer 23:5; 33:15; Chv 5:5
  • +Nu 24:17; Chv 2:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 317-318

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/2000, tsa. 14

    8/15/1994, tsa. 31

Chivumbulutso 22:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 21:9
  • +Yoh 4:14
  • +Yes 55:1; Yoh 7:37; Chv 7:17; 21:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2015, ptsa. 28-29

    12/15/2011, tsa. 25

    2/15/2010, ptsa. 14-18

    6/1/2008, ptsa. 14-15

    2/15/1998, ptsa. 18-19, 24

    9/1/1993, tsa. 32

    2/1/1992, tsa. 18

    12/15/1990, ptsa. 10-15

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 310-311, 318

    Kukambitsirana, tsa. 117

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 111-112

Chivumbulutso 22:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 4:2; 12:32; Aga 1:8; 1Yo 4:3; 2Yo 9
  • +Chv 15:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 318-319

Chivumbulutso 22:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:7
  • +Chv 21:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 318-319

Chivumbulutso 22:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:11; 22:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2007, tsa. 3

    12/1/1999, tsa. 19

    12/15/1994, tsa. 24

    Tsiku la Yehova, ptsa. 156-157

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 319

Chivumbulutso 22:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 319

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 22:1Eze 47:1
Chiv. 22:1Yoh 1:29
Chiv. 22:2Eze 47:12
Chiv. 22:3Chv 3:21
Chiv. 22:4Mt 5:8
Chiv. 22:4Chv 14:1
Chiv. 22:5Chv 21:25
Chiv. 22:5Yes 60:19, 20; 1Yo 1:5
Chiv. 22:5Da 7:18; Chv 3:21
Chiv. 22:6Tit 1:2
Chiv. 22:62Ti 3:16
Chiv. 22:7Chv 16:15; 22:20
Chiv. 22:7Yoh 13:17; Chv 1:3
Chiv. 22:9Mt 4:10; Mac 10:25, 26; Chv 19:10
Chiv. 22:12Sl 62:12; Yes 40:10; Aro 2:6
Chiv. 22:13Yes 44:6; 48:12; Chv 1:8; 21:6
Chiv. 22:141Yo 1:7
Chiv. 22:14Chv 2:7
Chiv. 22:14Chv 21:10, 12
Chiv. 22:15Aga 5:19-21; Aef 5:5; Chv 21:8
Chiv. 22:16Yes 11:1, 10; 53:2; Yer 23:5; 33:15; Chv 5:5
Chiv. 22:16Nu 24:17; Chv 2:28
Chiv. 22:17Chv 21:9
Chiv. 22:17Yoh 4:14
Chiv. 22:17Yes 55:1; Yoh 7:37; Chv 7:17; 21:6
Chiv. 22:18De 4:2; 12:32; Aga 1:8; 1Yo 4:3; 2Yo 9
Chiv. 22:18Chv 15:1
Chiv. 22:19Chv 2:7
Chiv. 22:19Chv 21:2
Chiv. 22:20Chv 3:11; 22:7
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 22:1-21

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa.+ 2 Mtsinjewo unadutsa pakati pa msewu waukulu wamumzindawo. Kumbali zonse ziwiri za mtsinjewo kunali mitengo ya moyo imene inkabereka zipatso zokolola maulendo 12, ndipo inkabereka zipatso mwezi uliwonse. Masamba a mitengoyo anali ochiritsira mitundu ya anthu.+

3 Mulungu sadzatembereranso mzindawo. Koma mpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa+ udzakhala mumzindamo ndipo akapolo a Mulungu adzachita utumiki wopatulika kwa iye. 4 Iwo adzaona nkhope yake+ ndipo dzina lake lidzakhala pazipumi zawo.+ 5 Komanso, usiku sudzakhalakonso+ ndipo sadzafunikiranso kuwala kwa nyale kapena kwa dzuwa, chifukwa Yehova* Mulungu adzawaunikira.+ Ndipo iwo adzalamulira monga mafumu mpaka kalekale.+

6 Iye anandiuza kuti: “Mawu awa ndi odalirika ndiponso oona.+ Yehova,* Mulungu amene anauzira aneneri+ kuti apereke mauthenga, watumiza mngelo wake kuti adzaonetse akapolo ake zinthu zimene zikuyenera kuchitika posachedwa. 7 Taonani! Ndikubwera mofulumira.+ Wosangalala ndi aliyense amene akutsatira mawu a ulosi amumpukutuwu.”+

8 Ine Yohane, ndi amene ndinamva komanso kuona zinthu zimenezi. Nditamva komanso kuona zinthu zimenezi, ndinagwada nʼkuwerama pamapazi a mngelo amene ankandionetsa zinthu zimenezi kuti ndimulambire. 9 Koma iye anandiuza kuti: “Samala! Usachite zimenezo! Inetu ndangokhala kapolo mnzako, kapolo wa aneneri amene ndi abale ako komanso wa anthu amene akutsatira mawu amumpukutu umenewu. Lambira Mulungu.”+

10 Anandiuzanso kuti: “Usasunge mwachinsinsi mawu a ulosi amumpukutuwu, chifukwa nthawi yoikidwiratu yayandikira. 11 Amene akuchita zosalungama, apitirize kuchita zosalungamazo ndipo amene akuchita zonyansa apitirizebe kuchita zonyansazo. Koma wolungama apitirize kuchita zachilungamo ndipo woyera apitirize kukhala woyera.

12 ‘Taonani! Ndikubwera mofulumira ndipo ndili ndi mphoto yoti ndipereke kwa aliyense mogwirizana ndi ntchito yake.+ 13 Ine ndine Alefa ndi Omega,*+ woyamba ndi wotsiriza, chiyambi ndi mapeto. 14 Osangalala ndi amene achapa mikanjo yawo+ kuti akhale ndi ufulu wodya zipatso zamʼmitengo ya moyo,+ ndiponso kuti aloledwe kulowa mumzindawo kudzera pamageti ake.+ 15 Kunja kuli anthu amene ali ngati agalu* komanso amene amachita zamizimu, achiwerewere,* opha anthu, olambira mafano ndi aliyense amene amakonda kunama komanso kuchita zachinyengo.’+

16 ‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kuti adzachitire umboni zinthu zimenezi kwa iwe kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu komanso mbadwa ya Davide.+ Ndinenso nthanda yowala kwambiri.’”+

17 Mzimu ndi mkwatibwi+ akupitiriza kunena kuti, “Bwera!” ndipo aliyense amene wamva anene kuti, “Bwera!” Komanso aliyense amene akumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi opatsa moyo kwaulere.+

18 “Ine ndikuchitira umboni kwa aliyense amene wamva mawu a ulosi wamumpukutuwu kuti: Wina akawonjezera pa zimenezi,+ Mulungu adzamuwonjezera miliri imene yalembedwa mumpukutuwu.+ 19 Ndipo wina akachotsa kalikonse pa mawu amumpukutu wa ulosi umenewu, Mulungu adzachotsa gawo lake pa zimene zalembedwa mumpukutuwu. Kutanthauza kuti sadzamulola kudya zipatso zamʼmitengo ya moyo+ komanso sadzamulola kulowa mumzinda woyerawo.+

20 Amene akuchitira umboni zinthu zimenezi akuti, ‘Inde, ndikubwera mofulumira.’”+

“Ame! Bwerani, Ambuye Yesu.”

21 Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu kukhale ndi oyerawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena