Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 12
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Machitidwe 12:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Ameneyu anali Herode Agiripa Woyamba.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 15:20; Mac 4:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 77-78

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2007, tsa. 22

Machitidwe 12:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 4:21
  • +Mt 20:23; Lu 11:49

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 78

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 11

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:27
  • +Eks 12:15; 23:15; Le 23:6

Machitidwe 12:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 21:12; Mac 5:18
  • +Eks 12:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 77-78

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 11

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 1:11; Aef 6:18; 1At 5:17; Yak 5:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 78-79

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, ptsa. 11-12

Machitidwe 12:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 77, 79-80

Machitidwe 12:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 34:7; Ahe 1:14
  • +1Mf 19:7
  • +Mac 16:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 12

Machitidwe 12:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 5:19
  • +Mko 10:50

Machitidwe 12:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:5

Machitidwe 12:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 83

Machitidwe 12:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 34:7; Da 3:28; 6:22; Ahe 1:14
  • +2Pe 2:9

Machitidwe 12:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:5; 15:37; Akl 4:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 18, 80, 118

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2010, ptsa. 6-7

    2/1/2008, tsa. 24

    3/1/2000, tsa. 16

Machitidwe 12:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 80-81

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2010, tsa. 7

Machitidwe 12:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 80-81

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 48:16; Mt 18:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 80-81

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/2005, tsa. 31

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:16; 19:33
  • +Mt 13:55; Mac 15:13; 21:18; 1Ak 15:7; Aga 1:19; 2:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 81, 112

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1997, tsa. 16

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 5:21

Machitidwe 12:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 12:6
  • +Mac 16:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 81

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 5:9; Eze 27:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 81-82

    Galamukani!,

    4/2011, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 28:2; Yuda 16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/1/1998, tsa. 30

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Sa 24:17; 2Mb 32:21
  • +Yes 42:8; 1Ak 1:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 82

    Galamukani!,

    4/2011, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1990, tsa. 20

Machitidwe 12:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 55:11; Mac 6:7; 19:20
  • +Akl 1:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 82

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/2001, ptsa. 10, 11-12

Machitidwe 12:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 4:36
  • +Mac 11:29
  • +Mac 13:5; 15:37

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 118

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2010, tsa. 7

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 12:1Yoh 15:20; Mac 4:3
Mac. 12:2Mt 4:21
Mac. 12:2Mt 20:23; Lu 11:49
Mac. 12:3Mac 24:27
Mac. 12:3Eks 12:15; 23:15; Le 23:6
Mac. 12:4Lu 21:12; Mac 5:18
Mac. 12:4Eks 12:11
Mac. 12:52Ak 1:11; Aef 6:18; 1At 5:17; Yak 5:16
Mac. 12:7Sl 34:7; Ahe 1:14
Mac. 12:71Mf 19:7
Mac. 12:7Mac 16:26
Mac. 12:8Mac 5:19
Mac. 12:8Mko 10:50
Mac. 12:9Mac 11:5
Mac. 12:10Mac 16:26
Mac. 12:11Sl 34:7; Da 3:28; 6:22; Ahe 1:14
Mac. 12:112Pe 2:9
Mac. 12:12Mac 13:5; 15:37; Akl 4:10
Mac. 12:15Ge 48:16; Mt 18:10
Mac. 12:17Mac 13:16; 19:33
Mac. 12:17Mt 13:55; Mac 15:13; 21:18; 1Ak 15:7; Aga 1:19; 2:9
Mac. 12:18Mac 5:21
Mac. 12:19Mac 12:6
Mac. 12:19Mac 16:27
Mac. 12:201Mf 5:9; Eze 27:17
Mac. 12:22Eze 28:2; Yuda 16
Mac. 12:232Sa 24:17; 2Mb 32:21
Mac. 12:23Yes 42:8; 1Ak 1:29
Mac. 12:24Yes 55:11; Mac 6:7; 19:20
Mac. 12:24Akl 1:6
Mac. 12:25Mac 4:36
Mac. 12:25Mac 11:29
Mac. 12:25Mac 13:5; 15:37
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 12:1-25

Machitidwe

12 Nthawi imeneyo m’pamene Mfumu Herode* anayamba kuzunza+ ena a mumpingo. 2 Yakobo m’bale wake wa Yohane+ anamupha ndi lupanga.+ 3 Ataona kuti zimenezi zasangalatsa Ayuda,+ anamanganso Petulo. (Amenewa anali masiku a mikate yopanda chofufumitsa.)+ 4 Atamugwira, anamutsekera m’ndende+ ndipo anamupereka m’manja mwa magulu anayi a asilikali, kuti azisinthana pomulondera. Gulu lililonse linali ndi asilikali anayi. Cholinga cha Herode chinali chakuti adzamuonetse kwa anthu pambuyo pa pasika.+ 5 Chotero Petulo anakhala akusungidwa m’ndendemo, koma mpingo unali kumupempherera+ mosalekeza kwa Mulungu ndi mtima wonse.

6 Tsopano Herode atakonzeka kuti abweretse Petulo kwa anthu, usiku umenewo Petuloyo anali chigonere ali womangidwa ndi maunyolo awiri pakati pa asilikali awiri. Pakhomo panalinso alonda olondera ndende. 7 Mwadzidzidzi, mngelo wa Yehova anaimirira+ chapafupi, ndipo kuwala kunaunika m’chipinda cha ndendecho. Kenako mngeloyo anadzutsa Petulo mwa kumugunda m’nthiti,+ n’kunena kuti: “Dzuka msanga!” Pamenepo maunyolo amene anamumanga nawo manjawo anagwa pansi.+ 8 Ndiyeno mngeloyo+ anamuuza kuti: “Konzeka ndipo uvale nsapato zako.” Iye anachita zimenezo. Kenako anamuuza kuti: “Vala malaya ako akunja+ ndipo uzinditsatira.” 9 Pamenepo anatuluka ndi kumamutsatira, koma iye sanadziwe kuti zimene zinali kuchitika ndi mngelozo zinali zenizeni. Ankangoganiza kuti akuona masomphenya.+ 10 Atapitirira gulu loyamba la asilikali a pachipata ndi lachiwiri, anafika pachipata chachitsulo cholowera mumzinda, ndipo chinawatsegukira chokha.+ Pamene anatuluka anayendera limodzi msewu umodzi wokha, ndipo nthawi yomweyo mngelo uja anamuchokera. 11 Koma Petulo nzeru zitamubwerera, anati: “Ndadziwa tsopano kuti Yehova ndiye watumiza mngelo wake+ kudzandilanditsa+ m’manja mwa Herode, komanso kudzandilanditsa ku zonse zimene anthu achiyuda anali kuyembekezera.”

12 Ataganizira zimene zinachitikazo, iye anapita kunyumba ya Mariya, mayi wake wa Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana pamodzi ndipo anali kupemphera. 13 Pamene anagogoda pachitseko cha pachipata, mtsikana wantchito dzina lake Roda anapita kuti akaone amene akugogoda. 14 Koma atazindikira mawu a Petulo, sanatsegule chipatacho chifukwa cha chimwemwe. M’malomwake, anathamangira mkati ndi kukanena kuti Petulo waima pachipata. 15 Iwo anamunena kuti: “Wachita misala eti!” Koma iye analimbikira kunena motsimikiza kuti akunena zoona. Iwo tsopano anayamba kunena kuti: “Ndi mngelo wake ameneyo.”+ 16 Koma Petulo anapitiriza kugogoda. Iwo atatsegula, anamuona ndipo anadabwa kwambiri. 17 Koma iye anawakwezera dzanja+ kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova anamutulutsira m’ndende. Kenako iye anati: “Zinthu zimenezi mukazifotokoze kwa Yakobo+ ndi kwa abale.” Atatero anatuluka n’kupita kumalo ena.

18 Tsopano kutacha,+ panali chipwirikiti pakati pa asilikali aja posadziwa chimene chachitikira Petulo. 19 Herode+ anafunafuna Petulo pena paliponse, ndipo atalephera kumupeza, anapanikiza alondawo ndi mafunso ndi kulamula kuti awatenge, akawapatse chilango.+ Pamenepo Herode anachoka ku Yudeya ndi kupita ku Kaisareya, kumene anakhalako kanthawi ndithu.

20 Tsopano Herode anali wokwiya ndi anthu a ku Turo ndi ku Sidoni, ndipo anafuna kuwathira nkhondo. Choncho onse anabwera kwa iye mogwirizana. Ndipo iwo atanyengerera Balasito, amene anali woyang’anira chipinda chogona cha mfumu, anayamba kupempha mtendere. Iwo anachita zimenezi chifukwa dziko lawo linali kudalira chakudya+ chochokera m’dziko la mfumuyo. 21 Koma pa tsiku loikidwiratu, Herode anavala zovala zake zachifumu ndi kukhala pampando wake woweruzira milandu, ndi kuyamba kulankhula nawo. 22 Anthu osonkhanawo atamva mawu ake anayamba kufuula kuti: “Amenewa ndi mawu a mulungu, osati a munthu ayi!”+ 23 Nthawi yomweyo mngelo wa Yehova anamukantha,+ chifukwa sanapereke ulemerero kwa Mulungu.+ Ndipo anadyedwa ndi mphutsi n’kumwalira.

24 Koma mawu+ a Yehova anapitiriza kukula ndi kufalikira.+

25 Tsopano Baranaba+ ndi Saulo atamaliza utumiki wopereka thandizo+ ku Yerusalemu, anabwerera ndi kutenga Yohane,+ wotchedwanso Maliko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena