Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 19
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Tamandani Ya chifukwa cha ziweruzo zake (1-10)

        • Ukwati wa Mwanawankhosa (7-9)

      • Amene anakwera pahatchi yoyera (11-16)

      • Phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo (17, 18)

      • Chilombo chinagonjetsedwa (19-21)

Chivumbulutso 19:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “Aleluya!” “Ya” ndi chidule cha dzina lakuti Yehova.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 150:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 272

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, tsa. 16

Chivumbulutso 19:2

Mawu a M'munsi

  • *

    MʼChigiriki por·nei′a. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

  • *

    Mʼchilankhulo choyambirira, “amene ali mʼmanja mwake.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +De 32:4; Sl 19:9; Chv 15:3
  • +De 32:43; 2Mf 9:7; Sl 79:10; Chv 18:20, 24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 272

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1989, tsa. 16

Chivumbulutso 19:3

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “Aleluya!” “Ya” ndi chidule cha dzina lakuti Yehova.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 117:1
  • +Yes 34:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 272-273

Chivumbulutso 19:4

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “Aleluya!” “Ya” ndi chidule cha dzina lakuti Yehova.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:4
  • +Chv 4:6
  • +Sl 106:48

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 273-274

Chivumbulutso 19:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 134:1; 135:1
  • +Sl 115:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 274

Chivumbulutso 19:6

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “Aleluya!” “Ya” ndi chidule cha dzina lakuti Yehova.

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 113:1
  • +Eks 6:3
  • +Sl 97:1; Yes 52:7; Chv 11:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 274-275

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1993, ptsa. 25-26

    12/15/1990, tsa. 16

    7/1/1989, ptsa. 23-24

Chivumbulutso 19:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2014, tsa. 22

    2/15/2014, ptsa. 8-12

    7/1/1995, ptsa. 13-14

    5/1/1993, tsa. 26

    8/15/1990, tsa. 31

    8/15/1989, tsa. 29

    7/1/1989, ptsa. 23-24

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 276-277

Chivumbulutso 19:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 61:10; Aef 5:25-27; Chv 14:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 276

Chivumbulutso 19:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 22:2; 25:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2015, tsa. 19

    2/15/2014, ptsa. 10-11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 72, 277-278

Chivumbulutso 19:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:25, 26; Chv 22:8, 9
  • +Mt 28:19, 20; Mac 1:8
  • +Mt 4:10; Yoh 4:23
  • +Lu 24:27; Mac 10:43; 1Pe 1:10, 11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2009, tsa. 5

    5/1/1987, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 278-279

Chivumbulutso 19:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:2
  • +Chv 1:5
  • +Yoh 1:14; Chv 3:14
  • +Yes 11:4, 5; Ahe 1:8, 9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 17

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 280

Chivumbulutso 19:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:13, 14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 65, 280-281

Chivumbulutso 19:13

Mawu a M'munsi

  • *

    Mabaibulo ena amati, “anawazidwa.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 1:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 281

Chivumbulutso 19:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 17

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2014, ptsa. 6-7

    2/15/2009, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 281

Chivumbulutso 19:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2At 2:8; Chv 1:13, 16
  • +Sl 2:9; Chv 2:26, 27
  • +Yow 3:13; Chv 14:19, 20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 282-284

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1990, ptsa. 4-5

Chivumbulutso 19:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 28:18; Afi 2:9-11; 1Ti 6:15; Chv 17:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 284

Chivumbulutso 19:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 39:4, 17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 284-285

Chivumbulutso 19:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 39:18
  • +Eze 39:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 13, 284-285

Chivumbulutso 19:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:14, 16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2020, tsa. 15

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2015, tsa. 29

    3/15/2007, tsa. 4

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 285-286

Chivumbulutso 19:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 16:13
  • +Chv 13:16, 17
  • +Chv 13:15
  • +Mt 10:28; 2Pe 2:6; Yuda 7; Chv 20:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 11

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2148

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 285-286

Chivumbulutso 19:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:16; 6:2
  • +Eze 39:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 285-286

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 19:1Sl 150:6
Chiv. 19:2De 32:4; Sl 19:9; Chv 15:3
Chiv. 19:2De 32:43; 2Mf 9:7; Sl 79:10; Chv 18:20, 24
Chiv. 19:3Sl 117:1
Chiv. 19:3Yes 34:10
Chiv. 19:4Chv 4:4
Chiv. 19:4Chv 4:6
Chiv. 19:4Sl 106:48
Chiv. 19:5Sl 134:1; 135:1
Chiv. 19:5Sl 115:13
Chiv. 19:6Sl 113:1
Chiv. 19:6Eks 6:3
Chiv. 19:6Sl 97:1; Yes 52:7; Chv 11:15
Chiv. 19:8Yes 61:10; Aef 5:25-27; Chv 14:4
Chiv. 19:9Mt 22:2; 25:10
Chiv. 19:10Mac 10:25, 26; Chv 22:8, 9
Chiv. 19:10Mt 28:19, 20; Mac 1:8
Chiv. 19:10Mt 4:10; Yoh 4:23
Chiv. 19:10Lu 24:27; Mac 10:43; 1Pe 1:10, 11
Chiv. 19:11Chv 6:2
Chiv. 19:11Chv 1:5
Chiv. 19:11Yoh 1:14; Chv 3:14
Chiv. 19:11Yes 11:4, 5; Ahe 1:8, 9
Chiv. 19:12Chv 1:13, 14
Chiv. 19:13Yoh 1:1
Chiv. 19:152At 2:8; Chv 1:13, 16
Chiv. 19:15Sl 2:9; Chv 2:26, 27
Chiv. 19:15Yow 3:13; Chv 14:19, 20
Chiv. 19:16Mt 28:18; Afi 2:9-11; 1Ti 6:15; Chv 17:14
Chiv. 19:17Eze 39:4, 17
Chiv. 19:18Eze 39:18
Chiv. 19:18Eze 39:20
Chiv. 19:19Chv 16:14, 16
Chiv. 19:20Chv 16:13
Chiv. 19:20Chv 13:16, 17
Chiv. 19:20Chv 13:15
Chiv. 19:20Mt 10:28; 2Pe 2:6; Yuda 7; Chv 20:14
Chiv. 19:21Chv 2:16; 6:2
Chiv. 19:21Eze 39:4
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 19:1-21

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu kumwamba amene ankamveka ngati mawu ofuula a khamu lalikulu akuti: “Tamandani Ya!*+ Mulungu wathu amapulumutsa anthu ndipo ali ndi mphamvu zazikulu komanso ulemerero, 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi chiwerewere* chake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”*+ 3 Nthawi yomweyo, ananenanso kachiwiri kuti: “Tamandani Ya!*+ Utsi umene ukufuka chifukwa cha kuwotchedwa kwake udzafuka mpaka kalekale.”+

4 Ndiye akulu 24+ ndi angelo 4 aja,+ anagwada pansi nʼkuwerama ndipo analambira Mulungu amene wakhala pampando wachifumu, nʼkunena kuti: “Ame! Tamandani Ya!”*+

5 Komanso kumpando wachifumu kunamveka mawu akuti: “Muzitamanda Mulungu wathu, inu nonse akapolo ake,+ amene mumamuopa, olemekezeka ndi onyozeka omwe.”+

6 Kenako ndinamva mawu amene ankamveka ngati mawu a khamu lalikulu, ngati mkokomo wa madzi ambiri komanso ngati mabingu amphamvu. Mawuwo anali akuti: “Tamandani Ya!*+ chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu!+ 7 Tiyeni tisangalale ndipo tikhale ndi chimwemwe chodzaza tsaya komanso timupatse ulemerero, chifukwa ukwati wa Mwanawankhosa wafika ndipo mkazi wake wadzikongoletsa. 8 Iye waloledwa kuti avale zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, chifukwa zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+

9 Mngeloyo anandiuza kuti, “Lemba kuti: Osangalala ndi amene aitanidwa kuchakudya chamadzulo cha phwando la ukwati wa Mwanawankhosa.”+ Anandiuzanso kuti: “Amenewa ndi mawu oona a Mulungu.” 10 Zitatero ndinagwada pansi nʼkuwerama patsogolo pa mapazi ake kuti ndimulambire. Koma iye anandiuza kuti: “Samala! Usachite zimenezo!+ Inetu ndangokhala kapolo mnzako ndi wa abale ako amene ali ndi ntchito yochitira umboni za Yesu.+ Lambira Mulungu,+ chifukwa cholinga cha maulosi ndi kuchitira umboni zokhudza Yesu.”+

11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+ 12 Maso ake anali ngati lawi la moto+ ndipo pamutu pake panali zisoti zachifumu zambiri. Iye analembedwa dzina limene palibe wina aliyense amene akulidziwa koma iye yekha. 13 Iye anavala malaya akunja amene anadonthera* magazi, ndipo amadziwika ndi dzina lakuti Mawu+ a Mulungu. 14 Komanso magulu ankhondo akumwamba ankamutsatira atakwera mahatchi oyera, atavala zovala zapamwamba, zoyera bwino, za mbee! 15 Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali+ lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Komanso iye ankapondaponda muchopondera mphesa cha mkwiyo waukulu wa Mulungu Wamphamvuyonse.+ 16 Pamalaya ake akunja komanso pantchafu yake, panalembedwa dzina lakuti, Mfumu ya mafumu ndi Mbuye wa ambuye.+

17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame zonse zouluka chapafupi mumlengalenga kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni kuphwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,+ 18 kuti mudzadye minofu ya mafumu, ya akuluakulu a asilikali, ya amuna amphamvu,+ ya mahatchi ndi ya amene akwera pamahatchiwo,+ minofu ya onse, ya mfulu ndi ya akapolo, ya olemekezeka ndi ya onyozeka.”

19 Ndiyeno ndinaona chilombo, mafumu a dziko lapansi ndi asilikali awo atasonkhana pamodzi kuti amenyane ndi amene anakwera pahatchi uja ndi gulu lake lankhondo.+ 20 Koma chilombocho chinagwidwa limodzi ndi mneneri wabodza+ uja, amene anachita zizindikiro pamaso pa chilombocho. Zizindikiro zimenezi anasocheretsa nazo amene analandira chizindikiro cha chilombo+ komanso amene ankalambira chifaniziro chake.+ Onse awiri adakali amoyo, anaponyedwa mʼnyanja ya moto yoyaka ndi sulufule.+ 21 Koma ena onse anaphedwa ndi lupanga lalitali limene linkatuluka mʼkamwa mwa amene anakwera pahatchi+ uja. Ndipo mbalame zonse zinakhuta minofu yawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena