Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 18
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 18:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 12:10
  • +Mt 17:2; Chv 1:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 259

Chivumbulutso 18:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 50:2
  • +Yes 21:9; Yer 51:8; Chv 14:8
  • +Sl 39:5
  • +Yes 13:21; Yer 50:39; 51:37

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 58

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 259-261

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, ptsa. 3-5

    4/15/1989, tsa. 9

Chivumbulutso 18:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 51:7
  • +Yes 47:5; Chv 17:2
  • +Yes 23:8
  • +Miy 19:10; Yes 47:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 261-264

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1989, ptsa. 4-5

Chivumbulutso 18:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 48:20; 52:11; Yer 50:8; 51:45; Zek 2:7
  • +Yer 51:6; 2Ak 6:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 16-17

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2006, ptsa. 28-29

    10/1/2005, tsa. 24

    4/15/1999, ptsa. 28-30

    4/15/1989, ptsa. 7-9

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

    Galamukani!,

    11/8/1996, ptsa. 8-9

    Mtendere Weniweni, tsa. 32

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 32-35

Chivumbulutso 18:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 51:9; 1Ti 5:24
  • +Yer 51:49, 56; Chv 16:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

Chivumbulutso 18:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2At 1:6
  • +Sl 137:8; Yer 50:15; 51:24
  • +Sl 75:8; Yer 51:7; Chv 16:19
  • +Chv 14:10
  • +Yer 17:18; 50:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

Chivumbulutso 18:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 50:29
  • +Chv 17:15
  • +Yes 47:8
  • +Sl 10:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

    Yesaya 2, tsa. 119

Chivumbulutso 18:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 50:13
  • +Le 21:9; Yer 51:58; Ahe 12:29
  • +Yer 50:34

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 265-266

    Yesaya 2, tsa. 119

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1989, tsa. 6

    Mtendere Weniweni, tsa. 32

Chivumbulutso 18:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 23:17
  • +Yer 50:46; Eze 27:35
  • +Chv 18:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 5

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 267

Chivumbulutso 18:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 26:17
  • +Da 4:30
  • +Yer 51:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 267

Chivumbulutso 18:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 27:36
  • +Eze 27:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268

Chivumbulutso 18:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 27:12
  • +Eze 27:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2009, tsa. 23

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268

Chivumbulutso 18:13

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “zonunkhiritsa zochokera ku India.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 27:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/2009, tsa. 23

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268

Chivumbulutso 18:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ti 6:10
  • +Mla 5:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 267-268

Chivumbulutso 18:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 27:36
  • +Eze 27:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 268

Chivumbulutso 18:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 27:31
  • +Chv 17:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 268

Chivumbulutso 18:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 11:4
  • +Yes 23:14
  • +Eze 27:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 268

Chivumbulutso 18:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 27:32

Chivumbulutso 18:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Sa 4:12
  • +Eze 27:30
  • +Eze 27:9
  • +Eze 27:33
  • +Yes 47:11; Yer 51:55

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 268

Chivumbulutso 18:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 51:48; Chv 12:12
  • +Chv 14:12
  • +1Ak 4:9
  • +De 32:43; Aro 12:19; Chv 6:10; 19:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 268-269

Chivumbulutso 18:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 18:6
  • +Yer 51:63
  • +Yer 51:64; Eze 26:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 13

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 269

Chivumbulutso 18:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 24:8; Eze 26:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 269-270

Chivumbulutso 18:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 25:10
  • +Yes 23:8
  • +Mko 6:21
  • +Yes 47:9; Aga 5:20; Chv 9:21

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 269-270

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1989, ptsa. 6-7

    4/1/1989, tsa. 4

Chivumbulutso 18:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 6:10
  • +Mt 23:37
  • +Chv 16:6
  • +Ge 9:6; Yer 51:49

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2006, tsa. 28

    2/1/1990, ptsa. 17-20

    5/15/1989, tsa. 5

    5/1/1989, tsa. 6

    4/15/1989, tsa. 23

    4/1/1989, ptsa. 4-5, 8-9

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 270-271

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 18:1Chv 12:10
Chiv. 18:1Mt 17:2; Chv 1:16
Chiv. 18:2Yer 50:2
Chiv. 18:2Yes 21:9; Yer 51:8; Chv 14:8
Chiv. 18:2Sl 39:5
Chiv. 18:2Yes 13:21; Yer 50:39; 51:37
Chiv. 18:3Yer 51:7
Chiv. 18:3Yes 47:5; Chv 17:2
Chiv. 18:3Yes 23:8
Chiv. 18:3Miy 19:10; Yes 47:1
Chiv. 18:4Yes 48:20; 52:11; Yer 50:8; 51:45; Zek 2:7
Chiv. 18:4Yer 51:6; 2Ak 6:17
Chiv. 18:5Yer 51:9; 1Ti 5:24
Chiv. 18:5Yer 51:49, 56; Chv 16:19
Chiv. 18:62At 1:6
Chiv. 18:6Sl 137:8; Yer 50:15; 51:24
Chiv. 18:6Sl 75:8; Yer 51:7; Chv 16:19
Chiv. 18:6Chv 14:10
Chiv. 18:6Yer 17:18; 50:21
Chiv. 18:7Yer 50:29
Chiv. 18:7Chv 17:15
Chiv. 18:7Yes 47:8
Chiv. 18:7Sl 10:6
Chiv. 18:8Yer 50:13
Chiv. 18:8Le 21:9; Yer 51:58; Ahe 12:29
Chiv. 18:8Yer 50:34
Chiv. 18:9Yes 23:17
Chiv. 18:9Yer 50:46; Eze 27:35
Chiv. 18:9Chv 18:18
Chiv. 18:10Eze 26:17
Chiv. 18:10Da 4:30
Chiv. 18:10Yer 51:8
Chiv. 18:11Eze 27:36
Chiv. 18:11Eze 27:30
Chiv. 18:12Eze 27:12
Chiv. 18:12Eze 27:22
Chiv. 18:13Eze 27:13
Chiv. 18:141Ti 6:10
Chiv. 18:14Mla 5:10
Chiv. 18:15Eze 27:36
Chiv. 18:15Eze 27:30
Chiv. 18:16Eze 27:31
Chiv. 18:16Chv 17:4
Chiv. 18:17Miy 11:4
Chiv. 18:17Yes 23:14
Chiv. 18:17Eze 27:27
Chiv. 18:18Eze 27:32
Chiv. 18:191Sa 4:12
Chiv. 18:19Eze 27:30
Chiv. 18:19Eze 27:9
Chiv. 18:19Eze 27:33
Chiv. 18:19Yes 47:11; Yer 51:55
Chiv. 18:20Yer 51:48; Chv 12:12
Chiv. 18:20Chv 14:12
Chiv. 18:201Ak 4:9
Chiv. 18:20De 32:43; Aro 12:19; Chv 6:10; 19:2
Chiv. 18:21Mt 18:6
Chiv. 18:21Yer 51:63
Chiv. 18:21Yer 51:64; Eze 26:21
Chiv. 18:22Yes 24:8; Eze 26:13
Chiv. 18:23Yer 25:10
Chiv. 18:23Yes 23:8
Chiv. 18:23Mko 6:21
Chiv. 18:23Yes 47:9; Aga 5:20; Chv 9:21
Chiv. 18:24Chv 6:10
Chiv. 18:24Mt 23:37
Chiv. 18:24Chv 16:6
Chiv. 18:24Ge 9:6; Yer 51:49
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 18:1-24

Chivumbulutso

18 Zimenezi zitatha, ndinaona mngelo wina akutsika kumwamba wokhala ndi ulamuliro+ waukulu. Ndipo dziko lapansi linawala ndi ulemerero wake.+ 2 Iye anafuula ndi mawu amphamvu,+ akuti: “Wagwa! Babulo Wamkulu wagwa,+ ndipo wakhala malo okhala ziwanda, ndiponso obisalamo mpweya+ uliwonse wonyansa wotuluka m’kamwa, komanso obisalamo mbalame iliyonse yonyansa ndi yodedwa.+ 3 Iye wamwetsa mitundu yonse ya anthu+ vinyo wa mkwiyo, vinyo wa dama lake. Ndipo mafumu a dziko lapansi anachita naye dama.+ Amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zambiri zamtengo wapatali zimene mkazi ameneyu anadziunjikira mopanda manyazi.”+

4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake. 5 Pakuti machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira+ zochita zake zopanda chilungamo. 6 M’bwezereni monga mmene iye anachitira.+ M’chitireni mowirikiza kawiri. Ndithu, wirikizani kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ M’kapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho+ kuwirikiza kawiri.+ 7 Pa muyezo umene anadzipezera ulemerero ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, pa muyezo womwewo mumuzunze ndi kumuliritsa.+ Pakuti mumtima mwake akumanena kuti, ‘Ine ndine mfumukazi.+ Sindine mkazi wamasiye,+ ndipo sindidzalira+ ngakhale pang’ono.’ 8 Ndiye chifukwa chake m’tsiku limodzi, miliri yake idzafika. Miliri yakeyo+ ndiyo imfa, kulira, ndi njala. Ndipo adzanyekeratu ndi moto+ chifukwa Yehova Mulungu, amene anamuweruza, ndi wamphamvu.+

9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake. 10 Ndipo ataima patali poona kuzunzika kwake, adzati,+ ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe!+ Babulo iwe, mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi, chiweruzo chako chafika!’+

11 “Komanso, amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi adzamulira+ maliro ndi kumva chisoni, chifukwa palibenso wina wowagula katundu wawo yense, 12 katundu yense+ wagolide, siliva, mwala wamtengo wapatali, ndi ngale. Komanso palibe wowagula nsalu zabwino kwambiri, zofiirira, zasilika, zofiira kwambiri, ndi mtengo uliwonse wa fungo lokoma, komanso chilichonse chopangidwa ndi mnyanga, chilichonse chopangidwa ndi mtengo wapamwamba, ndi chamkuwa, chachitsulo, ndi chamwala wa mabo.+ 13 Komanso palibe wowagula sinamoni, amomo,* zofukiza, mafuta onunkhira, lubani, vinyo, mafuta a maolivi, ufa wabwino kwambiri, tirigu, ng’ombe, nkhosa, mahatchi, ngolo, akapolo, ndi anthu.+ 14 Zoonadi, chipatso chabwino chimene moyo wako unali kulakalaka+ chakuchokera. Zinthu zako zonse zabwino ndi zokongola zawonongeka, ndipo anthu sadzazipezanso.+

15 “Amalonda oyendayenda+ a zinthu zimenezi, amene analemerera pa iye, adzaima patali chifukwa cha mantha poona kuzunzika kwake. Iwo adzamulira maliro ndi kumva chisoni+ 16 ndipo azidzati, ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe+ wovala zovala zapamwamba, zofiirira, ndi zofiira kwambiri. Mzinda wokongoletsedwa mochititsa kaso iwe, ndi zokongoletsera zagolide, zamwala wamtengo wapatali, ndi zangale.+ 17 Zachisoni, chifukwa mu ola limodzi, chuma chochulukachi chawonongedwa!’+

“Woyendetsa ngalawa aliyense ndi munthu aliyense woyenda panyanja kuchokera kulikonse,+ ogwira ntchito m’ngalawa ndi onse oyenda panyanja pochita malonda awo, anaima patali.+ 18 Poona utsi wofuka chifukwa cha kupsa kwake, iwo anafuula kuti, ‘Ndi mzinda uti ungafanane ndi mzinda waukulu+ umenewu?’ 19 Iwo anathira fumbi pamitu pawo+ akufuula, kulira ndi kumva chisoni,+ ndipo anati, ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwu, umene unalemeretsa+ onse okhala ndi ngalawa panyanja+ chifukwa cha chuma chake chamtengo wapatali, pakuti mu ola limodzi, wawonongedwa.’+

20 “Kondwerani kumwambako+ chifukwa cha zimene zamuchitikira. Inunso oyera,+ inu atumwi,+ ndi inu aneneri, kondwerani chifukwa Mulungu wamuweruza ndi kumupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+

21 Ndiyeno mngelo wamphamvu ananyamula mwala wooneka ngati mphero yaikulu+ n’kuuponya m’nyanja,+ ndipo anati: “Mzinda waukulu wa Babulo udzaponyedwa pansi mofulumira ndi mwamphamvu chonchi, ndipo sudzapezekanso.+ 22 Pamenepo kuimba kwa oimba motsagana ndi zeze, kwa oimba zitoliro, kwa oimba malipenga, ndi kwa oimba ena, sikudzamvekanso+ mwa iwe. Mwa iwe simudzapezekanso mmisiri wa ntchito iliyonse, ngakhale phokoso la mphero silidzamvekanso mwa iwe. 23 Kuwala kwa nyale sikudzaunikanso mwa iwe. Mawu a mkwati ndi a mkwatibwi sadzamvekanso+ mwa iwe, chifukwa amalonda ako oyendayenda+ anali anthu apamwamba+ padziko lapansi, ndiponso mitundu yonse ya anthu inasocheretsedwa ndi zochita zako zamizimu.+ 24 Mwa iye munapezeka magazi+ a aneneri,+ a oyera,+ ndi a onse amene anaphedwa padziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena