Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 11:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 40:3
  • +1Ak 3:16; 2Ak 6:16; Aef 2:21; 1Pe 2:5; 4:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    10/15/1988, ptsa. 12-13

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2150, 2241

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 161-162

Chivumbulutso 11:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 40:17
  • +Lu 21:24
  • +Ahe 12:22; Chv 21:2
  • +Chv 13:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    10/15/1988, tsa. 13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 162-163

Chivumbulutso 11:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 8:17
  • +Mac 2:17; Chv 19:10
  • +Sl 69:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    8/1/1994, tsa. 31

    11/1/1993, ptsa. 9-10

    2/1/1986, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 164

    Ulosi wa Danieli, ptsa. 295-296

Chivumbulutso 11:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zek 4:3, 11
  • +Zek 4:12; Mt 5:14
  • +Zek 4:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 164

Chivumbulutso 11:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 5:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    5/15/1997, tsa. 12

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 164-166

Chivumbulutso 11:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 4:25
  • +1Mf 17:1; Yak 5:17
  • +Ge 9:4; Eks 7:19; Mac 15:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    5/15/1997, tsa. 12

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 164-165, 166-167, 208

Chivumbulutso 11:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:1
  • +Chv 2:10, 13; 12:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2020, tsa. 6

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    10/15/1988, tsa. 13

    7/1/1987, tsa. 21

    6/15/1987, ptsa. 15-16

    2/1/1986, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 167-169

Chivumbulutso 11:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 1:10
  • +Lu 13:33; Ahe 13:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 167-169

Chivumbulutso 11:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 13:7; 17:15
  • +Chv 11:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 167-169

Chivumbulutso 11:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 35:15; Miy 24:17
  • +Lu 23:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    2/1/1986, ptsa. 12-13

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 167-168

Chivumbulutso 11:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 11:9
  • +Eze 37:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    12/2019, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2014, tsa. 30

    10/15/1988, tsa. 13

    7/1/1987, tsa. 22

    6/15/1987, tsa. 16

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 168-170

Chivumbulutso 11:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 29:4
  • +Sl 50:5; 147:2; Chv 4:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 169-170, 199

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1987, tsa. 22

Chivumbulutso 11:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 6:13
  • +Yes 26:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 170-171

Chivumbulutso 11:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 9:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158, 171

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/1988, ptsa. 13-14

Chivumbulutso 11:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:6
  • +1Mb 29:11; Sl 22:28; 97:1; Da 4:17, 34; Chv 12:10
  • +Sl 2:6; Eze 21:27; Da 7:13; Lu 1:33; 22:29; 2Pe 1:11
  • +Sl 145:13; Da 2:44

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158, 171-172, 176

    Lambirani Mulungu, ptsa. 93-94

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/1990, tsa. 19

    1/15/1990, ptsa. 19-20

    4/1/1989, ptsa. 19-20

    12/15/1988, ptsa. 13-14

    Kukambitsirana, tsa. 129

Chivumbulutso 11:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 4:10; 14:3
  • +Sl 95:6
  • +Chv 7:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 172-173

Chivumbulutso 11:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 12:1
  • +Eks 6:3; Amo 4:13; Chv 16:7
  • +Eks 3:14; Chv 1:4; 16:5
  • +Eks 9:16; Yob 37:23; Yes 40:26; Aro 9:17; Chv 4:11
  • +Sl 99:1; Zek 14:9; Chv 19:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 172-173, 176

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1993, ptsa. 25-26

Chivumbulutso 11:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 4:16; Ahe 11:6; Chv 14:13
  • +Ho 12:10; Amo 3:7; Mt 2:23; Mac 3:18; Aro 1:2; Ahe 1:1; Yak 5:10; 1Pe 1:10
  • +Sl 115:13; Mac 26:22
  • +Yes 6:11; Yer 4:7; 26:18; Mik 3:12
  • +Ge 6:11; Sl 53:1; Yer 6:28; 51:25; Zef 3:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nkhani Zina, article 55

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/2015, ptsa. 6-7

    9/1/2014, ptsa. 3-4, 6

    5/1/2011, tsa. 8

    3/1/1993, ptsa. 5-6

    4/1/1991, ptsa. 6-7

    7/1/1990, ptsa. 3-4, 5-6

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 173-176

    Galamukani!,

    11/8/1993, tsa. 32

    2/8/1993, ptsa. 21-26, 27-29

    3/8/1992, ptsa. 20-21

    11/8/1991, ptsa. 12-14

    6/8/1990, tsa. 27

    4/8/1990, tsa. 29

    2/8/1990, tsa. 31

    5/8/1988, ptsa. 11-12

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 137

    Mtendere Weniweni, ptsa. 16-17, 97

Chivumbulutso 11:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 14:17
  • +1Mf 8:1; Sl 132:8
  • +Hab 2:20; Ahe 8:2; 9:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 175-176

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 11:1Eze 40:3
Chiv. 11:11Ak 3:16; 2Ak 6:16; Aef 2:21; 1Pe 2:5; 4:17
Chiv. 11:2Eze 40:17
Chiv. 11:2Lu 21:24
Chiv. 11:2Ahe 12:22; Chv 21:2
Chiv. 11:2Chv 13:5
Chiv. 11:3Yoh 8:17
Chiv. 11:3Mac 2:17; Chv 19:10
Chiv. 11:3Sl 69:11
Chiv. 11:4Zek 4:3, 11
Chiv. 11:4Zek 4:12; Mt 5:14
Chiv. 11:4Zek 4:14
Chiv. 11:5Yer 5:14
Chiv. 11:6Lu 4:25
Chiv. 11:61Mf 17:1; Yak 5:17
Chiv. 11:6Ge 9:4; Eks 7:19; Mac 15:20
Chiv. 11:7Chv 13:1
Chiv. 11:7Chv 2:10, 13; 12:17
Chiv. 11:8Yes 1:10
Chiv. 11:8Lu 13:33; Ahe 13:12
Chiv. 11:9Chv 13:7; 17:15
Chiv. 11:9Chv 11:11
Chiv. 11:10Sl 35:15; Miy 24:17
Chiv. 11:10Lu 23:12
Chiv. 11:11Chv 11:9
Chiv. 11:11Eze 37:5
Chiv. 11:12Sl 29:4
Chiv. 11:12Sl 50:5; 147:2; Chv 4:1
Chiv. 11:13Yes 6:13
Chiv. 11:13Yes 26:16
Chiv. 11:14Chv 9:12
Chiv. 11:15Chv 8:6
Chiv. 11:151Mb 29:11; Sl 22:28; 97:1; Da 4:17, 34; Chv 12:10
Chiv. 11:15Sl 2:6; Eze 21:27; Da 7:13; Lu 1:33; 22:29; 2Pe 1:11
Chiv. 11:15Sl 145:13; Da 2:44
Chiv. 11:16Chv 4:10; 14:3
Chiv. 11:16Sl 95:6
Chiv. 11:16Chv 7:11
Chiv. 11:17Yes 12:1
Chiv. 11:17Eks 6:3; Amo 4:13; Chv 16:7
Chiv. 11:17Eks 3:14; Chv 1:4; 16:5
Chiv. 11:17Eks 9:16; Yob 37:23; Yes 40:26; Aro 9:17; Chv 4:11
Chiv. 11:17Sl 99:1; Zek 14:9; Chv 19:6
Chiv. 11:181At 4:16; Ahe 11:6; Chv 14:13
Chiv. 11:18Ho 12:10; Amo 3:7; Mt 2:23; Mac 3:18; Aro 1:2; Ahe 1:1; Yak 5:10; 1Pe 1:10
Chiv. 11:18Sl 115:13; Mac 26:22
Chiv. 11:18Yes 6:11; Yer 4:7; 26:18; Mik 3:12
Chiv. 11:18Ge 6:11; Sl 53:1; Yer 6:28; 51:25; Zef 3:7
Chiv. 11:19Chv 14:17
Chiv. 11:191Mf 8:1; Sl 132:8
Chiv. 11:19Hab 2:20; Ahe 8:2; 9:11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 11:1-19

Chivumbulutso

11 Ndiyeno ndinapatsidwa bango lokhala ngati ndodo+ ndipo ndinauzidwa kuti: “Nyamuka, kayeze nyumba yopatulika ya pakachisi+ wa Mulungu, guwa lansembe, ndi amene akulambira mmenemo. 2 Koma bwalo lakunja+ kwa nyumba yopatulika ya pakachisi ulisiye, usaliyeze m’pang’ono pomwe chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+ 3 Ndiyeno ndidzachititsa mboni zanga ziwiri+ kunenera+ kwa masiku 1,260, zitavala ziguduli.”+ 4 Mboni zimenezi zikuimiridwa ndi mitengo iwiri ya maolivi,+ ndi zoikapo nyale ziwiri,+ ndipo mbonizo zaimirira pamaso pa Ambuye wa dziko lapansi.+

5 Ngati wina aliyense akufuna kuzivulaza, moto umatuluka m’kamwa mwawo ndi kupsereza adani awo.+ Ngati wina angafune kuzivulaza, ayenera kuphedwa mwanjira imeneyi. 6 Mboni zimenezi zili ndi ulamuliro wotseka kumwamba+ kuti mvula isagwe+ m’masiku onse amene zikunenera. Zilinso ndi ulamuliro pamadzi, woti ziwasandutse magazi.+ Komanso zili ndi ulamuliro wokantha dziko lapansi ndi mliri wamtundu uliwonse, maulendo ambirimbiri mogwirizana ndi mmene zingafunire.

7 Zikamaliza kuchitira umboni wawo, chilombo chotuluka muphompho+ chidzachita nazo nkhondo, ndipo chidzazigonjetsa ndi kuzipha.+ 8 Mitembo yawo idzagona pamsewu waukulu mumzinda waukulu, umene mophiphiritsira ukutchedwa Sodomu+ ndi Iguputo, kumenenso Ambuye wawo anapachikidwa.+ 9 Mitundu ya anthu, mafuko, zinenero, ndi mayiko,+ adzayang’anitsitsa mitembo yawo masiku atatu ndi hafu,+ ndipo sadzalola kuti mitemboyo iikidwe m’manda. 10 Okhala padziko lapansi adzakondwera+ kwambiri ndi imfa yawoyo. Iwo adzatumizirana+ mphatso, chifukwa aneneri awiriwa anazunza okhala padziko lapansi.

11 Masiku atatu ndi hafu+ aja atatha, mzimu wa moyo wochokera kwa Mulungu unalowa mwa mboni zija.+ Ndiyeno mbonizo zinaimirira, ndipo amene anali kuziona anagwidwa ndi mantha aakulu. 12 Kenako mbonizo zinamva mawu ofuula+ ochokera kumwamba akuziuza kuti: “Kwerani kuno.”+ Ndipo zinakwera kumwamba mumtambo, moti adani awo anaziona. 13 Mu ola limenelo, kunachitika chivomezi chachikulu, ndipo gawo limodzi mwa magawo khumi+ a mzindawo linagwa. Anthu 7,000 anaphedwa ndi chivomezicho, ndipo ena onse anachita mantha n’kupereka ulemerero kwa Mulungu wakumwamba.+

14 Tsoka+ lachiwiri linapita. Koma tsoka lachitatu linali kubwera mofulumira.

15 Mngelo wa 7 analiza lipenga+ lake. Ndipo kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana, akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake.+ Iye adzalamulira monga mfumu kwamuyaya.”+

16 Ndipo akulu 24 aja,+ amene anali atakhala pamipando yawo yachifumu pamaso pa Mulungu, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo analambira Mulungu+ 17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+ 18 Koma mitundu ya anthu inakwiya, ndipo mkwiyo wanu unafika. Inafikanso nthawi yoikidwiratu yakuti akufa aweruzidwe, nthawi yopereka mphoto+ kwa akapolo anu aneneri,+ ndiponso kwa oyerawo, ndi oopa dzina lanu, olemekezeka ndi onyozeka omwe.+ Komanso, nthawi yowononga+ amene akuwononga dziko lapansi.”+

19 Nyumba yopatulika ya pakachisi wa Mulungu imene ili kumwamba+ inatsegulidwa, ndipo likasa+ la pangano lake linaonekera m’nyumba yake yopatulika+ ya pakachisi. Pamenepo kunachitika mphezi, kunamveka mawu, kunagunda mabingu, kunachita chivomezi, ndipo kunagwa matalala ambiri zedi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena