Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Machitidwe

      • Anatsutsana ku Antiokeya pa nkhani ya mdulidwe (1, 2)

      • Nkhaniyi anapita nayo ku Yerusalemu (3-5)

      • Akulu ndi atumwi anakumana kuti akambirane (6-21)

      • Kalata yochokera ku bungwe lolamulira (22-29)

        • Azipewa magazi (28, 29)

      • Mipingo inalimbikitsidwa ndi kalata (30-35)

      • Paulo ndi Baranaba anasiyana (36-41)

Machitidwe 15:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 17:9, 10; Eks 12:48; Le 12:2, 3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 101-102

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1998, tsa. 22

    5/15/1995, ptsa. 11-12

    6/15/1990, ptsa. 12-13

    2/15/1989, tsa. 19

Machitidwe 15:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 2:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 102-104

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/1997, tsa. 16

    5/15/1995, ptsa. 11-12

    2/15/1989, tsa. 19

    8/1/1987, tsa. 12

Machitidwe 15:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 104-105

Machitidwe 15:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 12:48; Mac 11:2, 3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 105, 107

Machitidwe 15:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 105-106

Machitidwe 15:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:34, 35; 11:16, 17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mb 28:9; Yer 11:20
  • +Mac 10:44, 45; 11:15

Machitidwe 15:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 3:28
  • +Aga 2:15, 16; 1Pe 1:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

Machitidwe 15:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 5:1
  • +Aga 3:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 53:11; Yoh 1:17
  • +Mt 20:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 106

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

Machitidwe 15:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 10:2; Mac 11:13; 2Pe 1:1
  • +1Pe 2:9, 10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 108-109

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    10/2021, ptsa. 20-21

    Gulu, tsa. 162

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2014, tsa. 16

    11/15/2014, ptsa. 24-25

    3/15/2013, ptsa. 27-28

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 108-109

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

Machitidwe 15:16

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “msasa; nyumba.”

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 109

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2013, ptsa. 8-9

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:17

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Amo 9:11, 12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 109

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2012, tsa. 5

Machitidwe 15:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 45:21

Machitidwe 15:19

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “maganizo.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 109-111

Machitidwe 15:20

Mawu a M'munsi

  • *

    MʼChigiriki por·nei′a. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

  • *

    Kapena kuti, “nyama imene yaphedwa osazinga kuti magazi atuluke.” Ena amati kusinga.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 35:2; Eks 20:3; 1Ak 10:14
  • +1Ak 6:9, 10; Akl 3:5; 1At 4:3
  • +Ge 9:4; Le 3:17; 7:26; 17:10, 13; 19:26; De 12:23; 15:23; 1Sa 14:32, 33

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Galamukani!,

    11/8/1990, tsa. 15

Machitidwe 15:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:15; 2Ak 3:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 109, 111

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/1995, tsa. 11

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 1:1; 1Pe 5:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 113

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/1999, ptsa. 26-27

Machitidwe 15:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 11:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 26

Machitidwe 15:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:1

Machitidwe 15:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:50; 1Ak 15:30, 31; 2Ak 11:23-26

Machitidwe 15:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:4

Machitidwe 15:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 16:13; Mac 5:32

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, tsa. 13

Machitidwe 15:29

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “nyama imene yaphedwa osazinga kuti magazi atuluke.” Ena amati kusinga.

  • *

    MʼChigiriki por·nei′a. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

  • *

    Kapena kuti, “moyo wathanzi.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 35:2; Eks 20:3; 34:15; 1Ak 10:14
  • +Ge 9:4; Le 3:17; 7:26; 17:10; De 12:16, 23; 1Sa 14:32, 33
  • +Le 17:13
  • +Ge 39:7-9; 1Ak 6:9, 10; Aef 5:5; Akl 3:5; 1At 4:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 39

    Mulungu Azikukondani, ptsa. 91-92

    Nsanja ya Olonda,

    12/15/2015, ptsa. 26-27

    6/15/2004, ptsa. 20-21, 29

    6/15/2000, tsa. 29

    1/15/1995, ptsa. 5-6

    6/15/1991, tsa. 9

    6/15/1990, tsa. 13

    6/1/1990, ptsa. 30-31

    3/1/1989, ptsa. 30-31

    5/1/1988, tsa. 17

    9/1/1986, tsa. 30

    3/15/1986, tsa. 15

    Zimene Baibulo Limaphunzitsa, ptsa. 139-140

    Baibulo Limaphunzitsa Chiyani, tsa. 130

    ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 77

    Mwazi, ptsa. 4-5, 20, 22

    Galamukani!,

    6/8/1990, tsa. 6

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 216

    Kukambitsirana, ptsa. 313, 315

Machitidwe 15:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

Machitidwe 15:31

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54

Machitidwe 15:32

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 114

Machitidwe 15:33

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 115

Machitidwe 15:34

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A3.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 115

Machitidwe 15:35

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Machitidwe 15:36

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 11:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 119

Machitidwe 15:37

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:4, 5; Akl 4:10; 2Ti 4:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 119-120

Machitidwe 15:38

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 120

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2010, tsa. 8

Machitidwe 15:39

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 4:36, 37

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 120

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/2011, tsa. 24

    3/15/2010, ptsa. 6, 8

    1/15/2003, ptsa. 19-20

    4/15/1998, ptsa. 22-23

    8/15/1993, ptsa. 21-22

    6/15/1990, ptsa. 13-14

    10/15/1989, tsa. 12

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 233-234

Machitidwe 15:40

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 14:26

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 15:1Ge 17:9, 10; Eks 12:48; Le 12:2, 3
Mac. 15:2Aga 2:1
Mac. 15:5Eks 12:48; Mac 11:2, 3
Mac. 15:7Mac 10:34, 35; 11:16, 17
Mac. 15:81Mb 28:9; Yer 11:20
Mac. 15:8Mac 10:44, 45; 11:15
Mac. 15:9Aga 3:28
Mac. 15:9Aga 2:15, 16; 1Pe 1:22
Mac. 15:10Aga 5:1
Mac. 15:10Aga 3:10
Mac. 15:11Yes 53:11; Yoh 1:17
Mac. 15:11Mt 20:28
Mac. 15:14Mt 10:2; Mac 11:13; 2Pe 1:1
Mac. 15:141Pe 2:9, 10
Mac. 15:17Amo 9:11, 12
Mac. 15:18Yes 45:21
Mac. 15:19Mac 15:10
Mac. 15:20Ge 35:2; Eks 20:3; 1Ak 10:14
Mac. 15:201Ak 6:9, 10; Akl 3:5; 1At 4:3
Mac. 15:20Ge 9:4; Le 3:17; 7:26; 17:10, 13; 19:26; De 12:23; 15:23; 1Sa 14:32, 33
Mac. 15:21Mac 13:15; 2Ak 3:15
Mac. 15:221At 1:1; 1Pe 5:12
Mac. 15:23Mac 11:26
Mac. 15:24Mac 15:1
Mac. 15:26Mac 13:50; 1Ak 15:30, 31; 2Ak 11:23-26
Mac. 15:27Mac 16:4
Mac. 15:28Yoh 16:13; Mac 5:32
Mac. 15:29Ge 35:2; Eks 20:3; 34:15; 1Ak 10:14
Mac. 15:29Ge 9:4; Le 3:17; 7:26; 17:10; De 12:16, 23; 1Sa 14:32, 33
Mac. 15:29Le 17:13
Mac. 15:29Ge 39:7-9; 1Ak 6:9, 10; Aef 5:5; Akl 3:5; 1At 4:3
Mac. 15:32Mac 18:23
Mac. 15:362Ak 11:28
Mac. 15:37Mac 13:4, 5; Akl 4:10; 2Ti 4:11
Mac. 15:38Mac 13:13
Mac. 15:39Mac 4:36, 37
Mac. 15:40Mac 14:26
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
  • 34
  • 35
  • 36
  • 37
  • 38
  • 39
  • 40
  • 41
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 15:1-41

Machitidwe a Atumwi

15 Ndiyeno amuna ena ochokera ku Yudeya anayamba kuphunzitsa abale kuti: “Mukapanda kudulidwa mogwirizana ndi mwambo wa Mose,+ simungapulumuke.” 2 Koma Paulo ndi Baranaba sanagwirizane nazo ndipo anatsutsana nawo. Choncho iwo anasankha Paulo, Baranaba komanso anthu ena, kuti apite kwa atumwi ndi akulu ku Yerusalemu+ kukawauza za nkhaniyi.

3 Mpingo utawaperekeza, anthu amenewa anapitiriza ulendo wawo kudzera ku Foinike ndi ku Samariya. Kumeneko ankafotokoza mwatsatanetsatane zoti anthu a mitundu ina ayamba kulambira Mulungu, ndipo abale onse anasangalala kwambiri ndi zimenezi. 4 Atafika ku Yerusalemu analandiridwa ndi manja awiri ndi mpingo, atumwi komanso akulu. Ndipo anafotokoza zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwowo. 5 Koma okhulupirira ena, amene kale anali mʼgulu lampatuko la Afarisi, anaimirira mʼmipando yawo nʼkunena kuti: “Mʼpofunika kuwadula komanso kuwalamula kuti azisunga Chilamulo cha Mose.”+

6 Choncho atumwi ndi akulu anasonkhana kuti akambirane za nkhani imeneyi. 7 Atatsutsana kwambiri za nkhaniyi, Petulo anaimirira nʼkuwauza kuti: “Abale anga, mukudziwa bwino kuti mʼmasiku oyambirira Mulungu anandisankha ine pakati panu, kuti kudzera pakamwa panga, anthu a mitundu ina amve mawu a uthenga wabwino nʼkukhulupirira.+ 8 Ndipo Mulungu, amene amadziwa zamumtima,+ anachitira umboni powapatsa mzimu woyera+ ngati mmene anachitiranso kwa ife. 9 Iye sanasiyanitse mʼpangʼono pomwe pakati pa ife ndi iwo.+ Koma anayeretsa mitima yawo chifukwa cha chikhulupiriro chawo.+ 10 Ndiye nʼchifukwa chiyani inu mukumuyesa Mulungu posenzetsa ophunzira goli+ limene makolo athu ngakhalenso ifeyo sitinathe kulisenza?+ 11 Koma tsopano tikukhulupirira kuti ife tidzapulumuka chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye Yesu,+ mofanananso ndi anthu amenewa.”+

12 Zitatero gulu lonselo linakhala chete, ndipo linayamba kumvetsera pamene Baranaba ndi Paulo ankafotokoza zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri zimene Mulungu anachita pakati pa anthu a mitundu ina kudzera mwa iwo. 13 Atamaliza kulankhula, Yakobo anayankha kuti: “Abale anga, ndimvetsereni. 14 Sumiyoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti pakati pawo atengepo anthu odziwika ndi dzina lake.+ 15 Ndipo zimenezi zikugwirizana ndi zimene aneneri analemba zakuti: 16 ‘Zimenezi zikadzatha ndidzabwerera nʼkumanganso tenti* ya Davide imene inagwa. Ndidzamanganso malo ogumuka a nyumbayo nʼkuikonzanso. 17 Ndidzachita zimenezi kuti anthu otsalawo afunefune Yehova* ndi mtima wonse. Amufunefune pamodzi ndi mitundu yonse ya anthu, anthu otchedwa ndi dzina langa, watero Yehova* amene akuchita zinthu zimenezi,+ 18 zomwe anatsimikiza kalekale kuti adzazichita.’+ 19 Choncho chigamulo* changa nʼchakuti, anthu a mitundu ina amene ayamba kulambira Mulungu, tisawavutitse.+ 20 Koma tiyeni tiwalembere kuti apewe zinthu zoipitsidwa ndi mafano,+ chiwerewere,*+ zopotola* ndi magazi.+ 21 Chifukwa kuyambira kalekale, anthu akhala akulalikira mumzinda ndi mzinda mawu ochokera mʼmabuku a Mose, popeza mabuku amenewa amawerengedwa mokweza mʼmasunagoge sabata lililonse.”+

22 Kenako atumwi ndi akulu pamodzi ndi mpingo wonse, anagwirizana zosankha amuna pakati pawo, kuti awatumize ku Antiokeya limodzi ndi Paulo ndi Baranaba. Choncho anasankha Yudasi wotchedwa Barasaba ndi Sila,+ omwe ankatsogolera abale. 23 Ndiyeno analemba kalata nʼkuwapatsira yonena kuti:

“Ife abale anu atumwi pamodzi ndi akulu, tikulembera inu abale athu ochokera mʼmitundu ina, amene muli ku Antiokeya,+ ku Siriya ndi ku Kilikiya: Landirani moni! 24 Tamva kuti ena ochokera pakati pathu akhala akukuvutitsani polankhula zinthu zokusokonezani,+ ngakhale kuti ife sitinawapatse malangizo aliwonse. 25 Choncho tonse tagwirizana kuti tisankhe amuna nʼkuwatumiza pamodzi ndi abale athu okondedwa, Baranaba ndi Paulo. 26 Anthu amenewa apereka miyoyo yawo chifukwa cha dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu.+ 27 Tikutumiza Yudasi ndi Sila, kuti iwonso adzakufotokozereni zinthu zomwezi ndi mawu apakamwa.+ 28 Chifukwa mzimu woyera+ komanso ifeyo taona kuti ndi bwino kuti tisakusenzetseni mtolo wolemera, kupatula zinthu zofunika zokhazi zomwe ndi 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola*+ ndi chiwerewere.*+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri, zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”*

30 Amuna amenewa atanyamuka, anapita ku Antiokeya. Kumeneko anasonkhanitsa gulu lonse la anthu nʼkuwapatsa kalatayo. 31 Ataiwerenga, anasangalala chifukwa cha mawu olimbikitsawo. 32 Popeza Yudasi ndi Sila analinso aneneri, anawakambira abalewo nkhani zambiri ndipo anawalimbikitsa.+ 33 Atakhala kumeneko kwakanthawi, abalewo anawaperekeza ndipo anabwerera mwamtendere kwa amene anawatuma. 34* ⁠—— 35 Koma Paulo ndi Baranaba anatsala ku Antiokeya. Iwo pamodzi ndi anthu enanso ambiri ankaphunzitsa komanso kulengeza uthenga wabwino wa mawu a Yehova.*

36 Patapita masiku, Paulo anauza Baranaba kuti: “Tiyeni tibwerere kumizinda yonse kumene tinalalikira mawu a Yehova* kuti tikachezere abale ndiponso tikawaone kuti ali bwanji.”+ 37 Baranaba ankafunitsitsa kuti atenge Yohane, wotchedwanso Maliko.+ 38 Koma Paulo anaona kuti si bwino kumutenga chifukwa ulendo wina Yohane anawasiya ku Pamfuliya ndipo sanapite nawo ku ntchitoyi.+ 39 Zitatero anakangana koopsa mpaka anasiyana. Baranaba+ anatenga Maliko ndipo anayenda ulendo wapamadzi kupita ku Kupuro. 40 Koma Paulo anasankha Sila, ndipo abale atamupempherera Pauloyo kuti Yehova* amusonyeze kukoma mtima kwakukulu, ananyamuka.+ 41 Iye anadzera ku Siriya ndi ku Kilikiya ndipo ankalimbikitsa mipingo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena