Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 11
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Machitidwe 11:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Zek 2:11; Lu 2:32; Mac 14:27

Machitidwe 11:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:45; Aga 2:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2003, tsa. 22

Machitidwe 11:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:12

Machitidwe 11:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:13

Machitidwe 11:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eze 4:14; Mt 15:11; Mac 10:14

Machitidwe 11:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:9

Machitidwe 11:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:16

Machitidwe 11:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:17

Machitidwe 11:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 16:13; Mac 10:19
  • +Mac 10:23; 15:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 71-72

Machitidwe 11:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 10:30

Machitidwe 11:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 16:30

Machitidwe 11:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 2:4

Machitidwe 11:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 3:11; Mko 1:8; Lu 3:16; Mac 1:5
  • +Yes 44:3; Yow 2:28; Yoh 1:33; Mac 2:17

Machitidwe 11:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:8; Aga 3:2
  • +Da 4:35; Mac 10:47

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 73

Machitidwe 11:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:14
  • +Lu 2:20; Mac 13:48; 14:27
  • +Yes 11:10; Mac 17:30; 20:21; Aro 10:12; 15:9

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/1996, tsa. 16

Machitidwe 11:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 8:1
  • +Mac 21:2
  • +Mac 21:3
  • +Mt 10:6

Machitidwe 11:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 6:1; 9:29
  • +Mko 13:10; Aef 3:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 74

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 24-25

    1/1/1989, tsa. 11

Machitidwe 11:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 1:66
  • +Mac 2:47; 9:35

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/1/1989, ptsa. 11-12

Machitidwe 11:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 4:36

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 25

Machitidwe 11:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 12:15
  • +3Yo 4
  • +Mac 13:43; 14:22

Machitidwe 11:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 2:47; 4:4; 5:14; 9:31

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 25

Machitidwe 11:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:39
  • +Mac 9:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 25

Machitidwe 11:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 9:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 74-76

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, ptsa. 25-26

    6/1/1990, tsa. 19

Machitidwe 11:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:1; 15:32; 1Ak 12:28; Aef 4:11

Machitidwe 11:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:10
  • +Mt 24:7; Lu 4:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    4/2023, tsa. 16

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 74-76

    Galamukani!,

    4/2011, ptsa. 11-12

    Nsanja ya Olonda,

    6/1/1990, ptsa. 19-20

    12/15/1989, tsa. 19

Machitidwe 11:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Le 25:35; Miy 3:27; Mac 24:17; Aro 15:26; 1Ak 16:1; Aga 2:10
  • +2Ak 8:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    4/15/1998, tsa. 21

Machitidwe 11:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 12:25; Aga 2:1

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 11:1Zek 2:11; Lu 2:32; Mac 14:27
Mac. 11:2Mac 10:45; Aga 2:12
Mac. 11:6Mac 10:12
Mac. 11:7Mac 10:13
Mac. 11:8Eze 4:14; Mt 15:11; Mac 10:14
Mac. 11:9Mac 15:9
Mac. 11:10Mac 10:16
Mac. 11:11Mac 10:17
Mac. 11:12Yoh 16:13; Mac 10:19
Mac. 11:12Mac 10:23; 15:7
Mac. 11:13Mac 10:30
Mac. 11:14Mac 16:30
Mac. 11:15Mac 2:4
Mac. 11:16Mt 3:11; Mko 1:8; Lu 3:16; Mac 1:5
Mac. 11:16Yes 44:3; Yow 2:28; Yoh 1:33; Mac 2:17
Mac. 11:17Mac 15:8; Aga 3:2
Mac. 11:17Da 4:35; Mac 10:47
Mac. 11:18Mac 21:14
Mac. 11:18Lu 2:20; Mac 13:48; 14:27
Mac. 11:18Yes 11:10; Mac 17:30; 20:21; Aro 10:12; 15:9
Mac. 11:19Mac 8:1
Mac. 11:19Mac 21:2
Mac. 11:19Mac 21:3
Mac. 11:19Mt 10:6
Mac. 11:20Mac 6:1; 9:29
Mac. 11:20Mko 13:10; Aef 3:8
Mac. 11:21Lu 1:66
Mac. 11:21Mac 2:47; 9:35
Mac. 11:22Mac 4:36
Mac. 11:23Ahe 12:15
Mac. 11:233Yo 4
Mac. 11:23Mac 13:43; 14:22
Mac. 11:24Mac 2:47; 4:4; 5:14; 9:31
Mac. 11:25Mac 21:39
Mac. 11:25Mac 9:30
Mac. 11:26Mac 9:2
Mac. 11:27Mac 13:1; 15:32; 1Ak 12:28; Aef 4:11
Mac. 11:28Mac 21:10
Mac. 11:28Mt 24:7; Lu 4:25
Mac. 11:29Le 25:35; Miy 3:27; Mac 24:17; Aro 15:26; 1Ak 16:1; Aga 2:10
Mac. 11:292Ak 8:12
Mac. 11:30Mac 12:25; Aga 2:1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 11:1-30

Machitidwe

11 Tsopano atumwi ndi abale amene anali mu Yudeya anamva kuti anthu a mitundu ina+ nawonso alandira mawu a Mulungu. 2 Choncho Petulo atapita ku Yerusalemu, olimbikitsa mdulidwe+ anayamba kutsutsana naye. 3 Iwo anali kumunena kuti anakalowa m’nyumba ya anthu osadulidwa ndi kudya nawo. 4 Pamenepo Petulo anayamba kuwafotokozera mwatsatanetsatane zimene zinachitika, kuti:

5 “Ndinali kupemphera mumzinda wa Yopa. Ndipo ndinayamba kuona masomphenya. M’masomphenyawo ndinaona chinthu chikutsika. Chinthucho chinali chooneka ngati chinsalu chachikulu chimene achigwira m’makona onse anayi, ndipo anali kuchitsitsa kuchokera kumwamba moti chinafika kwa ine. 6 Nditayang’anitsitsa m’chinthucho, ndinaonamo nyama za miyendo inayi zapadziko lapansi, zilombo zakutchire, zokwawa komanso mbalame zam’mlengalenga.+ 7 Ndinamvanso mawu akundiuza kuti, ‘Nyamuka Petulo, ipha udye!’+ 8 Koma ine ndinati, ‘Iyayi Ambuye, m’kamwa mwangamu simunalowepo choipitsidwa ndi chonyansa chilichonse chiyambire.’+ 9 Poyankha, mawu ochokera kumwambawo anamveka kachiwiri kuti, ‘Zinthu zimene Mulungu waziyeretsa usiyiretu kuzinena kuti n’zoipitsidwa.’+ 10 Mawu amenewo anamvekanso kachitatu, ndipo zonse zinakwezedwanso kumwamba.+ 11 Nthawi yomweyo, amuna atatu amene anatumidwa kwa ine kuchokera ku Kaisareya anaima panyumba imene tinali kukhala.+ 12 Chotero mzimu+ unandiuza kuti ndipite nawo, ndisakayikire ngakhale pang’ono. Pamenepo abale 6 awa anatsagana nane, ndipo tinakalowa m’nyumba ya munthuyo.+

13 “Iye anatiuza mmene anaonera mngelo ataimirira m’nyumba yake ndi kunena kuti, ‘Tuma anthu kuti apite ku Yopa akaitane Simoni wotchedwanso Petulo.+ 14 Iye adzalankhula nawe zinthu zimene zidzathandize iwe ndi banja lako lonse kupulumuka.’+ 15 Koma nditangoyamba kulankhula, mzimu woyera unawagwera monga mmene unachitiranso pa ife poyamba paja.+ 16 Zitatero ndinakumbukira mawu a Ambuye aja akuti, ‘Yohane anabatiza ndi madzi,+ koma inu mudzabatizidwa ndi mzimu woyera.’+ 17 Chotero ngati Mulungu anapereka mphatso yaulere imodzimodziyo kwa iwo, monga mmenenso anachitira kwa ife amene tinakhulupirira mwa Ambuye Yesu Khristu,+ ine ndine ndani kuti ndiletse Mulungu?”+

18 Tsopano pamene iwo anamva zimenezi, anangovomereza,+ ndipo anatamanda Mulungu+ kuti: “Chabwino, pamenepa ndiye kuti Mulungu wapereka mwayi kwa anthu a mitundu ina kuti iwonso alape ndi kudzapeza moyo.”+

19 Ndiyeno anthu amene anabalalika+ chifukwa cha chisautso chimene chinagwera Sitefano anayenda mpaka ku Foinike,+ ku Kupuro+ ndi ku Antiokeya. Ndipo sanali kulalikira mawu kwa wina aliyense koma kwa Ayuda okha.+ 20 Koma pakati pawo panali amuna ena a ku Kupuro ndi ku Kurene. Amenewa atafika ku Antiokeya anayamba kulankhula ndi anthu olankhula Chigiriki,+ ndipo anali kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa Ambuye Yesu.+ 21 Apanso, dzanja la Yehova+ linali nawo, ndipo ambiri amene anakhulupirira anatembenukira kwa Ambuye.+

22 Mpingo wa ku Yerusalemu unamva za iwo, ndipo unatumiza Baranaba+ kuti apite ku Antiokeya. 23 Atafika kumeneko ndi kuona kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu, anakondwera+ ndipo anayamba kulimbikitsa onse kuti apitirize kukhala okhulupirika kwa Ambuye motsimikiza mtima.+ 24 Baranaba anali munthu wabwino, wodzazidwa ndi mzimu woyera komanso wachikhulupiriro. Ndipo khamu lalikulu ndithu linakhulupirira Ambuye.+ 25 Kenako Baranaba anapita ku Tariso+ kukafufuza Saulo+ 26 ndipo atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Choncho iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko chaka chonse, ndipo anaphunzitsa anthu ambirimbiri. Ku Antiokeya, n’kumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+

27 M’masiku amenewa aneneri+ anapita ku Antiokeya kuchokera ku Yerusalemu. 28 Mmodzi wa iwo dzina lake Agabo,+ analosera mwa mzimu kuti padziko lonse lapansi kumene kuli anthu,+ padzagwa njala yaikulu. Izi zinachitikadi m’nthawi ya Kalaudiyo. 29 Chotero aliyense wa ophunzirawo, anatsimikiza mtima kutumiza thandizo+ lililonse limene akanatha+ kwa abale okhala ku Yudeya. 30 Ndipo anachitadi zimenezo mwa kutumiza thandizolo kwa akulu, kudzera mwa Baranaba ndi Saulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena