Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 18
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Machitidwe 18:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 148

Machitidwe 18:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:26; 1Ak 16:19; 2Ti 4:19
  • +Ahe 13:24
  • +Mac 11:28

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 137

    Galamukani!,

    4/2011, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2003, ptsa. 19-20

    12/15/1996, tsa. 22

    6/15/1990, ptsa. 18-19

    Mawu a Mulungu, tsa. 62

Machitidwe 18:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 20:34; 1Ak 4:12; 9:15; 1At 2:9; 2At 3:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 148-150

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/2012, tsa. 15

    3/1/2009, ptsa. 26-27

    11/15/2003, ptsa. 19-20

    12/15/1996, ptsa. 22-23

    12/1/1992, ptsa. 28-29

    6/15/1990, ptsa. 18-19

    11/15/1986, ptsa. 29-30

Machitidwe 18:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 4:23; Mac 13:14; 17:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/1999, tsa. 15

Machitidwe 18:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 15:27; 17:14
  • +Mac 16:1; 1At 3:6
  • +Mac 17:3; 28:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

    Utumiki wa Ufumu,

    4/2001, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1991, tsa. 28

Machitidwe 18:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Pe 4:4
  • +Mt 10:14; Mac 13:51
  • +1Mf 2:37; Eze 18:13; 33:4
  • +Eze 3:18; Mac 20:26
  • +Mac 13:46; 28:28; Aro 1:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, ptsa. 21-22

Machitidwe 18:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/1990, ptsa. 18-19

Machitidwe 18:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 1:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151

Machitidwe 18:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 22:43; Mac 23:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 152-153

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/1997, tsa. 11

Machitidwe 18:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 1:19; Mt 28:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 152-153

    Nsanja ya Olonda,

    11/1/1997, tsa. 11

Machitidwe 18:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:7; 19:38
  • +Mac 16:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 152-153

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Nsanja ya Olonda,

    5/1/2012, tsa. 23

    6/15/1990, tsa. 19

Machitidwe 18:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 24:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 153

Machitidwe 18:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 153

Machitidwe 18:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ti 6:4
  • +Mac 23:29; 25:19

Machitidwe 18:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 155

Machitidwe 18:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 1:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 153

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2008, tsa. 32

    6/15/1990, tsa. 19

Machitidwe 18:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Nu 6:18; Mac 21:23
  • +Aro 16:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 152, 154

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2008, tsa. 32

    6/15/1990, tsa. 19

Machitidwe 18:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 13:14; 17:2

Machitidwe 18:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 21:6
  • +Aro 1:10; 1Ak 4:19; Yak 4:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 160

Machitidwe 18:22

Mawu a M'munsi

  • *

    Zikuoneka kuti anapita ku Yerusalemu.

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 154

Machitidwe 18:23

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 1:2
  • +Mac 16:6
  • +Mac 14:22; 15:32

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 160

Machitidwe 18:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 19:1; 1Ak 1:12; 3:6
  • +1Ak 4:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, ptsa. 20-21

Machitidwe 18:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 12:11
  • +Mac 19:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2010, tsa. 11

    10/1/1996, ptsa. 20-21

Machitidwe 18:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 16:3; 1Ak 16:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 159

    Nsanja ya Olonda,

    6/15/2010, tsa. 11

    11/15/2003, ptsa. 18-19

    10/1/1996, tsa. 21

    6/15/1990, tsa. 19

Machitidwe 18:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 3:6
  • +Aef 2:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, tsa. 21

Machitidwe 18:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 24:27; 1Ak 15:3; 2Ti 3:16
  • +Ge 49:10; De 18:15; Sl 16:10; Yes 7:14; Mik 5:2; Mki 3:1; Mac 9:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1996, ptsa. 21-22

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Mac. 18:2Mac 18:26; 1Ak 16:19; 2Ti 4:19
Mac. 18:2Ahe 13:24
Mac. 18:2Mac 11:28
Mac. 18:3Mac 20:34; 1Ak 4:12; 9:15; 1At 2:9; 2At 3:10
Mac. 18:4Mt 4:23; Mac 13:14; 17:2
Mac. 18:5Mac 15:27; 17:14
Mac. 18:5Mac 16:1; 1At 3:6
Mac. 18:5Mac 17:3; 28:23
Mac. 18:61Pe 4:4
Mac. 18:6Mt 10:14; Mac 13:51
Mac. 18:61Mf 2:37; Eze 18:13; 33:4
Mac. 18:6Eze 3:18; Mac 20:26
Mac. 18:6Mac 13:46; 28:28; Aro 1:16
Mac. 18:81Ak 1:14
Mac. 18:9Lu 22:43; Mac 23:11
Mac. 18:10Yer 1:19; Mt 28:20
Mac. 18:12Mac 13:7; 19:38
Mac. 18:12Mac 16:19
Mac. 18:13Mac 24:5
Mac. 18:151Ti 6:4
Mac. 18:15Mac 23:29; 25:19
Mac. 18:171Ak 1:1
Mac. 18:18Nu 6:18; Mac 21:23
Mac. 18:18Aro 16:1
Mac. 18:19Mac 13:14; 17:2
Mac. 18:21Mac 21:6
Mac. 18:21Aro 1:10; 1Ak 4:19; Yak 4:15
Mac. 18:23Aga 1:2
Mac. 18:23Mac 16:6
Mac. 18:23Mac 14:22; 15:32
Mac. 18:24Mac 19:1; 1Ak 1:12; 3:6
Mac. 18:241Ak 4:6
Mac. 18:25Aro 12:11
Mac. 18:25Mac 19:3
Mac. 18:26Aro 16:3; 1Ak 16:19
Mac. 18:271Ak 3:6
Mac. 18:27Aef 2:8
Mac. 18:28Lu 24:27; 1Ak 15:3; 2Ti 3:16
Mac. 18:28Ge 49:10; De 18:15; Sl 16:10; Yes 7:14; Mik 5:2; Mki 3:1; Mac 9:22
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Machitidwe 18:1-28

Machitidwe

18 Zimenezi zitatha, Paulo anachoka ku Atene n’kupita ku Korinto. 2 Kumeneko anapeza Myuda wina dzina lake Akula,+ mbadwa ya ku Ponto. Iyeyu pamodzi ndi mkazi wake Purisikila, anali atafika chaposachedwa kuchokera ku Italiya,+ chifukwa Kalaudiyo+ anali atalamula Ayuda onse kuti achoke ku Roma. Choncho Paulo anapita kwa iwo. 3 Ndipo popeza kuti ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwira ntchito pamodzi,+ pakuti onse anali amisiri opanga mahema. 4 Komabe Paulo anali kukamba nkhani m’sunagoge+ sabata lililonse, ndipo anali kukopa Ayuda ndi Agiriki.

5 Tsopano Sila+ ndi Timoteyo+ atafika kuchokera ku Makedoniya, Paulo anatanganidwa kwambiri ndi ntchito yolalikira mawu a Mulungu. Iye anali kuchitira umboni kwa Ayuda ndi kuwatsimikizira kuti Yesu ndiyedi Khristu.+ 6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndi kulankhula monyoza,+ iye anakutumula zovala zake+ ndi kuwauza kuti: “Magazi anu+ akhale pamitu panu. Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira tsopano ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+ 7 Zitatero, iye anachoka pamenepo ndi kupita kunyumba ya munthu wina dzina lake Titiyo Yusito. Iyeyu anali wolambira Mulungu, ndipo nyumba yake inali moyandikana ndi sunagoge. 8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhala wokhulupirira mwa Ambuye, pamodzi ndi onse a m’banja lake. Ndipo Akorinto ambiri amene anamva uthenga wabwino anayamba kukhulupirira ndi kubatizidwa. 9 Komanso usiku, Ambuye anauza Paulo+ m’masomphenya kuti: “Usaope, pitiriza kulankhula. Usakhale chete, 10 chifukwa ine ndili nawe.+ Palibe munthu amene adzakukhudze ndi kukuvulaza, pakuti ndili ndi anthu ambiri mumzinda uno.” 11 Choncho anakhazikika kumeneko chaka ndi miyezi 6, akuwaphunzitsa mawu a Mulungu.

12 Tsopano pamene Galiyo anali bwanamkubwa+ wa Akaya, Ayuda ananyamuka mogwirizana ndi kuukira Paulo, ndipo anamutengera kumpando woweruzira milandu.+ 13 Kumeneko iwo anati: “Munthu uyu akukopa anthu kuti azipembedza Mulungu m’njira yosemphana ndi chilamulo.”+ 14 Koma pamene Paulo ankati azitsegula pakamwa, Galiyo anauza Ayudawo kuti: “Ayuda inu, chikanakhala cholakwa china, kapena pakanachitika chinachake choipa, ndithu ndikanaleza mtima ndi kukumverani. 15 Koma ngati nkhani yake ili yokhudza mikangano pa mawu, mayina+ ndi chilamulo+ chanu, zimenezo muthane nazo nokha. Ine sindikufuna kuti ndikhale woweruza nkhani zoterezi.” 16 Atatero anawapitikitsa kumpando woweruzira milanduwo. 17 Zitatero, onse anagwira Sositene,+ mtsogoleri wa sunagoge ndi kuyamba kumumenya pafupi ndi mpando woweruzira milanduwo. Koma Galiyo sanasamale zimenezo ngakhale pang’ono.

18 Koma Paulo atakhala kumeneko masiku ndithu, anatsanzikana ndi abalewo ndipo anapitiriza ulendo wake wa pamadzi kulowera ku Siriya. Pa ulendowu anatsagana ndi Purisikila ndi Akula. Paulo anameta tsitsi lake+ ku Kenkereya+ chifukwa cha lonjezo limene anachita. 19 Choncho onse anafika ku Efeso, ndipo anzakewo anawasiya kumeneko. Koma iye yekha analowa m’sunagoge+ ndi kuyamba kukambirana ndi Ayuda. 20 Ngakhale kuti anamupempha mobwerezabwereza kuti akhale nawo kwa nthawi yotalikirapo, iye sanalole. 21 M’malomwake, anatsanzikana+ nawo ndi kuwauza kuti: “Yehova akalola ndidzabweranso kudzakuonani.”+ Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wa panyanja 22 ndipo anafika ku Kaisareya. Kenako anapita* kukapereka moni ku mpingo, ndipo pambuyo pake anapita ku Antiokeya.

23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka ndi kuyenda malo osiyanasiyana m’chigawo cha Galatiya+ ndi Fulugiya,+ ndipo anali kulimbikitsa+ ophunzira onse.

24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ mbadwa ya ku Alekizandiriya, amene anali ndi mphatso ya kulankhula, anafika ku Efeso. Iyeyu analinso kuwadziwa bwino Malemba.+ 25 Mwamuna ameneyu analangizidwa njira ya Yehova ndi mawu a pakamwa. Ndiyeno popeza kuti anali wodzipereka kwambiri chifukwa chakuti anali ndi mzimu woyera,+ anali kulankhula ndi kuphunzitsa molondola za Yesu. Koma anali kudziwa za ubatizo+ wa Yohane wokha basi. 26 Mwamuna ameneyu anayamba kulankhula molimba mtima musunagoge. Tsopano Purisikila ndi Akula+ atamumvetsera, anamutenga ndi kumufotokozera njira ya Mulungu molondola. 27 Ndiponso, popeza kuti anali wofunitsitsa kupita ku Akaya, abalewo analembera ophunzira kumeneko. Anawalimbikitsa kuti amulandire ndi manja awiri. Choncho iye atafika kumeneko, anathandiza kwambiri+ anthu amene anali atakhulupirira chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.+ 28 Pakuti mwamphamvu, iye anawatsimikizira Ayuda poyera kuti anali olakwa, ndipo anasonyeza mwa Malemba+ kuti Yesu ndiyedi Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena