Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Zimene Zili Mʼbuku la Chivumbulutso

      • Chivumbulutso chochokera kwa Mulungu, kudzera mwa Yesu (1-3)

      • Moni wopita kumipingo 7 (4-8)

        • “Ine ndine Alefa ndi Omega” (8)

      • Atadzazidwa ndi mzimu woyera, Yohane anapezeka kuti ali mʼtsiku la Ambuye (9-11)

      • Masomphenya a Yesu, atalandira ulemerero (12-20)

Chivumbulutso 1:1

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “Kuulula; Kuvumbulutsa.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 2:28
  • +Amo 3:7; Chv 7:3, 4
  • +Mt 10:2; Mko 1:19; Yoh 21:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, tsa. 2

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 15-17

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, ptsa. 15, 19

    11/1/1999, tsa. 6

Chivumbulutso 1:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 16-17

Chivumbulutso 1:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 1:2; Lu 11:28; Yoh 13:17; Yak 1:22

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 31

    12/1/1999, ptsa. 14-19

    4/1/1989, ptsa. 10-11

    12/15/1988, ptsa. 10-11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 6, 17

Chivumbulutso 1:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:11
  • +Chv 1:8; 4:8; 11:17
  • +Chv 4:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 18

Chivumbulutso 1:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 3:14
  • +Akl 1:18
  • +Sl 89:27; 1Ti 6:15; Chv 19:16
  • +Yoh 15:9
  • +Ahe 9:14; 1Pe 1:18, 19; 1Yo 1:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 18-19

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, tsa. 10

Chivumbulutso 1:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 19:6; Lu 22:28-30
  • +1Pe 2:5; Chv 5:9, 10; 20:6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 19

Chivumbulutso 1:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 26:64; Mko 13:26
  • +Mt 24:30

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 226

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2007, ptsa. 3, 5

    5/1/1993, ptsa. 22-23

    10/1/1992, ptsa. 15-16

    1/1/1988, tsa. 18

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 19-20

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 146

    Kukambitsirana, ptsa. 163-164

Chivumbulutso 1:8

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “ndine A ndi Z.” Alefa ndi chilembo choyambirira cha afabeti ya Chigiriki ndipo Omega ndi chilembo chomalizira.

  • *

    Onani Zakumapeto A5.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 48:12; Chv 21:6; 22:13
  • +Eks 6:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2136

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, ptsa. 30-31

    12/1/1999, tsa. 10

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 20

Chivumbulutso 1:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 10:22; 2Ti 2:12
  • +Mt 24:9
  • +Lu 12:32
  • +Aro 8:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 20-21

    Nsanja ya Olonda,

    12/1/1999, ptsa. 14-15

Chivumbulutso 1:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    5/2022, ptsa. 2-3

    Yesu—Ndi Njira, tsa. 313

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 22-24

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 10

    12/15/1997, tsa. 11

    4/15/1991, ptsa. 26-27

    4/1/1989, ptsa. 11-12

    12/15/1988, tsa. 11

    10/15/1988, tsa. 10

Chivumbulutso 1:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 1:1; Chv 2:1
  • +Chv 2:8
  • +Chv 2:12
  • +Chv 2:18
  • +Chv 3:1
  • +Chv 3:7
  • +Chv 3:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, tsa. 30

    8/15/2007, ptsa. 9, 11

    4/1/1989, tsa. 11

    12/15/1988, tsa. 11

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 23-24

    ‘Dziko Lokoma’, tsa. 33

    Sukulu ya Utumiki Wateokalase (1999), ptsa. 15-16

    Kukambitsirana, tsa. 399

Chivumbulutso 1:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:20

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 25, 28-29

Chivumbulutso 1:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Da 7:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 25

Chivumbulutso 1:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 19:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 25

Chivumbulutso 1:15

Mawu a M'munsi

  • *

    Kapena kuti, “mkuwa.”

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 2:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 25-26

Chivumbulutso 1:16

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:20
  • +Yes 49:2
  • +Mt 17:1, 2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2012, tsa. 14

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 26-27, 28-29

Chivumbulutso 1:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 26:23; Akl 1:18; Chv 1:5
  • +Chv 2:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2009, ptsa. 30-31

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 26-28

Chivumbulutso 1:18

Mawu a M'munsi

  • *

    Amenewa ndi manda a anthu onse. Onani Matanthauzo a Mawu Ena.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 15:45
  • +1Pe 3:18
  • +Aro 6:9; 1Ti 6:16
  • +Mt 16:18; Yoh 6:54; 11:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 27-28

    Lambirani Mulungu, ptsa. 83-84

Chivumbulutso 1:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 24

Chivumbulutso 1:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 5:16; Afi 2:15

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    11/2019, tsa. 5

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2012, tsa. 14

    9/15/2010, tsa. 27

    1/15/2009, tsa. 30

    4/1/2007, tsa. 27

    5/15/2003, ptsa. 10-11

    3/15/2002, tsa. 14

    10/1/1988, tsa. 17

    8/1/1987, ptsa. 17-18

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 28-29, 136

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 1:1Da 2:28
Chiv. 1:1Amo 3:7; Chv 7:3, 4
Chiv. 1:1Mt 10:2; Mko 1:19; Yoh 21:20
Chiv. 1:3Sl 1:2; Lu 11:28; Yoh 13:17; Yak 1:22
Chiv. 1:4Chv 1:11
Chiv. 1:4Chv 1:8; 4:8; 11:17
Chiv. 1:4Chv 4:5
Chiv. 1:5Yoh 15:9
Chiv. 1:5Ahe 9:14; 1Pe 1:18, 19; 1Yo 1:7
Chiv. 1:5Chv 3:14
Chiv. 1:5Akl 1:18
Chiv. 1:5Sl 89:27; 1Ti 6:15; Chv 19:16
Chiv. 1:6Eks 19:6; Lu 22:28-30
Chiv. 1:61Pe 2:5; Chv 5:9, 10; 20:6
Chiv. 1:7Mt 26:64; Mko 13:26
Chiv. 1:7Mt 24:30
Chiv. 1:8Yes 48:12; Chv 21:6; 22:13
Chiv. 1:8Eks 6:3
Chiv. 1:9Mt 10:22; 2Ti 2:12
Chiv. 1:9Mt 24:9
Chiv. 1:9Lu 12:32
Chiv. 1:9Aro 8:17
Chiv. 1:11Aef 1:1; Chv 2:1
Chiv. 1:11Chv 2:8
Chiv. 1:11Chv 2:12
Chiv. 1:11Chv 2:18
Chiv. 1:11Chv 3:1
Chiv. 1:11Chv 3:7
Chiv. 1:11Chv 3:14
Chiv. 1:12Chv 1:20
Chiv. 1:13Da 7:13
Chiv. 1:14Chv 19:12
Chiv. 1:15Chv 2:18
Chiv. 1:16Chv 1:20
Chiv. 1:16Yes 49:2
Chiv. 1:16Mt 17:1, 2
Chiv. 1:17Mac 26:23; Akl 1:18; Chv 1:5
Chiv. 1:17Chv 2:8
Chiv. 1:181Ak 15:45
Chiv. 1:181Pe 3:18
Chiv. 1:18Aro 6:9; 1Ti 6:16
Chiv. 1:18Mt 16:18; Yoh 6:54; 11:25
Chiv. 1:20Mt 5:16; Afi 2:15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 1:1-20

Chivumbulutso Chimene Yohane Analandira

1 Chivumbulutso* chimene Yesu Khristu anapereka. Mulungu anamupatsa Chivumbulutso chimenechi+ kuti aonetse akapolo ake+ zinthu zimene zikuyenera kuchitika posachedwapa. Yesu anatumiza mngelo wake kuti adzapereke Chivumbulutsocho kwa kapolo wake Yohane+ pogwiritsa ntchito zizindikiro. 2 Yohaneyo anachitira umboni mawu amene Mulungu anapereka ndiponso umboni umene Yesu Khristu anapereka, kutanthauza zonse zimene anaona. 3 Wosangalala ndi munthu amene amawerenga mokweza komanso anthu amene akumva mawu a ulosi umenewu, ndiponso amene akutsatira zimene zalembedwa mmenemo,+ chifukwa nthawi yoikidwiratu yayandikira.

4 Ine Yohane, ndikulembera mipingo 7+ imene ili mʼchigawo cha Asia:

Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zikhale nanu kuchokera kwa “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera,”+ ndiponso kuchokera kwa mizimu 7+ imene ili pamaso pa mpando wake wachifumu. 5 Komanso kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa”+ ndiponso “Wolamulira mafumu a dziko lapansi.”+

Kwa iye amene amatikonda+ komanso amene anatimasula ku machimo athu pogwiritsa ntchito magazi ake,+ 6 nʼkutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kuti titumikire Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya. Ame.

7 Taonani! Akubwera ndi mitambo+ ndipo diso lililonse lidzamuona, ngakhalenso anthu amene anamubaya. Ndipo mafuko onse apadziko lapansi adzadziguguda pachifuwa pomva chisoni chifukwa cha iye.+ Inde, zimenezi zidzachitikadi. Ame.

8 “Ine ndine Alefa ndi Omega,”*+ akutero Yehova* Mulungu, “Iye amene alipo, amene analipo, ndi amene akubwera, Wamphamvuyonse.”+

9 Ine Yohane mʼbale wanu, amene mofanana ndi inu ndikupirira,+ ndikukumana ndi masautso+ ndipo tidzalamulira limodzi mu ufumu+ monga otsatira a Yesu,+ ndinali pachilumba cha Patimo chifukwa cholankhula za Mulungu ndi kuchitira umboni za Yesu. 10 Nditadzazidwa ndi mzimu woyera ndinapezeka kuti ndili mʼtsiku la Ambuye, ndipo kumbuyo kwanga ndinamva mawu amphamvu ngati kulira kwa lipenga. 11 Mawuwo anali akuti: “Zimene ukuona, uzilembe mumpukutu ndi kuutumiza kumipingo 7 yotsatirayi: wa ku Efeso,+ ku Simuna,+ ku Pegamo,+ ku Tiyatira,+ ku Sade,+ ku Filadefiya+ ndi wa ku Laodikaya.”+

12 Ndinacheuka kuti ndione kuti ndi ndani amene ankandilankhula. Nditacheuka, ndinaona zoikapo nyale 7 zagolide.+ 13 Pakati pa zoikapo nyalezo, panali wina wooneka ngati mwana wa munthu+ atavala chovala chofika kumapazi ndipo anali atamanga lamba wagolide pachifuwa. 14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera ngati ubweya woyera wa nkhosa, zinali zoyera kwambiri, ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+ 15 Mapazi ake anali ngati kopa* woyengedwa bwino+ amene akunyezimira mʼngʼanjo ndipo mawu ake ankamveka ngati mkokomo wa madzi ambiri. 16 Mʼdzanja lake lamanja anali ndi nyenyezi 7.+ Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali, lakuthwa konsekonse.+ Nkhope yake inali yowala ngati dzuwa limene likuwala kwambiri.+ 17 Nditamuona, ndinagwera pamapazi ake ngati kuti ndafa.

Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja nʼkundiuza kuti: “Usachite mantha. Ine ndine Woyamba+ ndi Womaliza,+ 18 ndiponso wamoyo.+ Ndinali wakufa,+ koma taona, ndili ndi moyo ndipo ndidzakhala ndi moyo mpaka kalekale,+ komanso ndili ndi makiyi a imfa ndi a Manda.*+ 19 Choncho lemba zimene waona, zimene zikuchitika panopa ndi zimene zichitike pambuyo pa zimenezi. 20 Koma za chinsinsi chopatulika cha nyenyezi 7 zimene waona mʼdzanja langa lamanja ndiponso za chinsinsi cha zoikapo nyale 7 zagolide, tanthauzo lake ndi ili: Nyenyezi 7 zikuimira angelo a mipingo 7, ndipo zoikapo nyale 7 zikuimira mipingo 7.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena